Why Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2021
Lyrics
Why - Eli Njuchi
...
Yeah Yeah
J max
J max
Njuchi
Savage
O yah yah
On the beat
Yeah Yeah
Dear ma hope
Ndalimba mtima lero Sangie
Sindikudziwa kuti zitha bwanji
Zomandiyankha
Pa Facebook,Insta,twitter nanji
Ma blue Tik onsewa bwanji
I have been following you
Mayi wa Ngwiro
Kuyambira form 1 mpaka 4
Every show ndi makhala konko
Sindinajombeko Sangie uku ndithera bundle
Kapena mwina
Chifukwa ndine mwana Sangie
Sizikugwirizana Sangie
Mesa tidzikondana
(Ndiyankhe Njuchi aku kakamileee)
Tell me why
Tell me why
Tell me why
Ndiyankhe Njuchi aku kakamile
Tell me why
Tell me why
Tell me why
Ndiyankhe Njuchi aku kakamile
Tikakumana kwa sespence
Hola yake ndi ayile basi
Singafile Njuchi alibe Vw
Akati watha mtunda ndi minbus
Ndikati ndi pemphe selfie
Uli busy
Ndikhole number
Ili busy
Mayi busy still I do it all for love
Ndiyankhe Njuchi aku aaah mxieew
Kapena mwina
Chifukwa ndine mwana Sangie
Sizikugwirizana Sangie
Mesa tidzikondana
(Ndiyankhe Njuchi aku kakamileee)
Tell me why
Tell me why
Tell me why
Ndiyankhe Njuchi aku kakamile
Tell me why
Tell me why
Tell me why (tell me why)
Ndiyankhe Njuchi aku kakamile
Tell me why (tell me why Sangie)
Tell me why (tell me why tell me why)
Tell me why
Ndiyankhe Njuchi aku kakamile
Tell me why (tell me whya)
Tell me why (tell me whya)
Tell me why
Ndiyankhe Njuchi aku kakamile
The End(@ausk)