Hane Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Hane - Eli Njuchi
...
Hane kubanja choka samachoka choncho
Hane pochoka ngati mukuthawa nkhondo
Hane wapambana
Ndikulila koto(hane wapambana)
Ndikulira koto
Hane kubanja choka samachoka choncho
Hane pochoka anasiya poto pamoto (hane wapambana)
Ndikulira koto(hane wapambana )
Ishi koma hane
Hane hane hane
Hane hane hane(hane wapambana)
Ndikulira hane(hane wapambana)
Ishi koma hane
Hane hane hane
Hane hane hane(hane wapambana)
Ndikulira hane(hane wapambana)
Ishi koma hane
Okay rrrr
Ati bwanji apa
Ishi koma hane utangochoka nkhawa moti zoona unasiya anawa
Ulipatsoka mawa
Chozemba chimakumana nchokwawa
Unagulitsa ng’ombe zanga zonse
Napinyulitsa njinga zanga zonse
Kunabweranso abanki nkonde
Akuti unatapira chingongole
Uli patsoka hane
Ndiwe njoka (hane)
Mnyumba mtsegule kunjoniku
Ndalama zanga unapangira chiphatso
Ishi koma hane
Hane hane hane
Hane hane hane (hane wapambana)