Loading...

Download
  • Genre:Others
  • Year of Release:2024

Lyrics

Tempolale - Eli Njuchi

...

Baby don't worry

usamaa dandaule

usamaa kayikile

ma tsikuwa uzilemba mu daily

mavutowa ndi history

zonsezi nzakale kale

chonde usazayiwaale

matsikuwa uzilemba mu daily

zonsezi ndiza tempolale

tempolale tempolale

matsikuwa uzilemba mu daily

zonsezi ndiza tempolale

mavuto anthuwa nga tempolale

misoziyathuyi tempolale

matsikuwa uzilemba mu daily

koopya tadusa kale

My lover

zachuma tamukumbukile yobuu my lover

za mwana tamukumbukile Salah my..

amalanda amapatsa usayiwale

my lover

taona zambiri kufika lelo my lover

nde ulova nka chani my lover

Kusowa ya rent nka chani my lover

kusowa ma fees nka chani my lover

zonsezi ndiza tempolale

mavuto anthuwa nga tempolale

misonzi yathu ija tempolale

matsikuwa uzilemba mu daily

zonsezi ndiza tempolale

mavuto anthuwa nga tempolale

misoziyathu ija tempolale

matsikuwa uzilemba mu daily

olo mdima uwopse bwanji

kunja kucha

Namodwe awombe bwanji tiza woloka

iwe ndi ineeee eeeeeh

olo mdima uwopse bwanji

kunja kucha

namodwe awombe bwanji tiza woloka

iwe ndi ineeee eeeh eeeh

iwe ndi ineeee eeeh eeeh

zonsezi ndiza tempolale

tempolale tempolale

matsikuwa uzilemba mu daily

zonsezi ndiza tempolale

mavuto anthuwa nga tempolale

misonzi yathu ija tempolale

matsikuwa uzilemba mu daily

Similar Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status