Loading...

Download
  • Genre:Afrobeats
  • Year of Release:2022

Lyrics

Bodza - Eli Njuchi

...

Njuchi

Eish koma yah!

Eish koma yah!


Verse 1

Munalowa bodza mu nyumbamo

Kuyambira makolo ndi anawo

Ndinampeza mpaka mgwanya wapa gate

Amalandira ma tip kwa azi uncle

Munalowa chi bodza mu nyumbamo

Kuyambira makolo ndi anawo

Makolo amangoti mwana ali ku geri

osadziwa anadya fees kalekale

Abambo amazivuta pa Malawi

akati akakatenge kapambali

Anafika pomasinthitsa galimoto

anthu asawazindikile mmakukamu

Amayi akuvutika pamalawi

akati akakholetse kapambali

Mtima umakhala uli panja ku gate

akangonva ka horn asuzumile


chorus

Koma palowa bodza bodza bodza pamalawi

Palowa bodza bodza bodza pamalawi

Bodza likutizunza pamalawi

Bodza likutiphetsa pamalawi

Palowa bodza bodza bodza pamalawi


verse 2

Mwalowa kunama mu mpingomu

Chopereka chanu mu mpingomu

chikumalowa purse ya chemwali

Chitukuko chapa church chagwera ena

Lero tipumeko za ndale, zandale takamba dzana kalekale

Kuja ndikuchimake kwa zonsezi

chitukuko chapa mudzi chagwera ena

Amachikunga chi bodza make Junior

ndili ku night service ali Bwandilo

Amachikunga chi bodza bambo awo

akati ataye ring kuma hotelo

Bea wakumbali mu telephone anasevedwa waterboard or ESCOM

Bea wakumbali mu telephone anasevedwa Champions league wina zamkhonde


Chorus

Ndati palowa bodza bodza bodza pamalawi

Palowa bodza bodza bodza pamalawi

Bodza likutizunza pamalawi

Bodza likutiphetsa pamalawi

Palowa bodza bodza bodza pamalawi


Verse 3

Ati akuphaka chi life pa social media

Handsome pa HD picture pokha

Tilipo ambiri okapsa

Akazi akufera bodza pamalawi


chorus

Ndati palowa bodza bodza bodza pamalawi

Palowa bodza bodza bodza pamalawi

Bodza likutizunza pamalawi Bodza likutiphetsa pamalawi

Palowa bodza bodza bodza pamalawi


Kwalowa bodza kumalawi

Similar Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status