Mije Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Mije - Eli Njuchi
...
...................
...savage
............(njuchi)
Pamtima panga
Pamazadumpha ndikava walowa mu mphanda, walowa m'nyumba
Ndi munthu wanga inde ndi banja komaso
munthuyu ndi mzanga, munthuyu ndi mzanga
Pali iyeyo...
kuseka sikushota ngati pali iyeyo
pali iyeyo, pali iyeyo
ndimadzidabwa ndekha ngati pali iyeyo
mwaifeyo (eeh!)
Muli mijedu , mijedu
ndife chi bank chankhani
mijedu ,mijedu
ndife chi bank chatinkhani
muli mijedu , mijedu
ndife chi bank chankhani
mijedu ,mijedu
ndife chi bank chiti nkhani
Tili ndikujeda, aneba nda nzao tinawaseka
Tili ndikujeda, tizibwezi ta nzake tasekedwa
Nde tikamaseka ,mpaka misozi m'masomu ...
Nde tikamaseka , mpaka nthiti kuwawa
Pali iyeyo...
kuseka sikushota ngati pali iyeyo
pali iyeyo, pali iyeyo .........................
Ndimadzidabwa ndekha ngati pali iyeyo
mwaifeyo (eeh!)
Muli mijedu , mijedu
Ndife chi bank chankhani
Mijedu ,mijedu
Ndife chi bank chatinkhani
muli mijedu , mijedu
ndife chi bank chankhani
mijedu ,mijedu
ndife chi bank chiti nkhani
Ngati tizasiyane
Ngati tizatayane
Mije ndizaisowa (mije ndizaisowa)
Ngati tizasiyane
Ngati tizatayane
Mije ndizaisowa (mije ndizaisowa)