Loading...

Download
  • Genre:R&B
  • Year of Release:2021

Lyrics

Ngati Iwe - Mazani

...

Oooh ooh

May inuyo anakonza

Nde zoti wina azikusewelesa kwa Ineyo sizoona

Nde mukuzuzikilanji mayi okongola ngati inu

Ngati inu

Nde ukuzunzikilanji mkazi okongola ngati iwe

Mwamuna wako ndiwansanje

Usakhale pa phone ati ukuyankhulana ndi ndani

Oooooh

Sizimuwaza ukakhala ndi anzako

Amaopa akuwuza chilungamo

Chomwe amachita iwe kulibeko

Ichi sichikondi

You have to let go

Nde umayenera chikondi chosefukila(kilA)

Nde Ukamalira pansi pa mtima uziziwa

Kuti uli ngati duwa

Akusamale (akusamale)

Akuthilile uwale eeeeh

Mayinuyo anakonza aaah

Nde zoti wina azikuseweresa kwa Ineyo sizoona

Nde ukuzunzilanji mkazi okongola ngati iwe(mkazi okongola ngati iwe)

Mkazi okongola ngati iwe(mkazi okongola ngati iwe)

Nde ukuzunzikilanji

Ukuzunzikilanji

Sungamusinthe ndi mmene Alili

Anayesapo ena zinavuta

Nde usakhalile kukhetsa misozi

Amuna abwino alipo

Kungotaya nthawi

Is he even worth it?

Akuwusewelesa Mwayi

Zochita zake ndizogwetsa mphwayi

Umayenera chikondi chosefukila

Nde ukamalila pansi pa mtima uziziwa

Kuti uli ngati duwa

Akusamale(akusamale)

Akuthilile uwale eeeeeh

Mayinuyo anakonza

Nde zoti wina azikuseweresa kwaineyo sizoona

Nde ukuzunzikilanji mkazi okongola ngati iwe(mkazi okongola ngati iwe)

Mkazi okongola ngati iwe (mkazi okongola ngati iwe)

Nde ukuzunzikilanji

Nde ukuzunzikilanji

Mayinuyo anakonza

Nde zoti wina azikuseweresa

Kwaineyo sizoona

Nde ukuzunzikilanji mkazi okongola ngati iwe (mkazi okongola ngati iwe)

Mkazi okongola ngati iwe (mkazi okongola ngati iwe)

Nde ukuzunzikilanji

Nde ukuzunzikilanji

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status