Loading...

Download
  • Genre:Others
  • Year of Release:2024

Lyrics

Timaso tako nditokomedwesa

Ndiwe okongola mosocheretsa

Ukamazima ndikusonkhetsera

Chikondi chimafuna kumvesesa

No tipekisi no correction

Iyi ni yane manifesto

I'll be your shield and protection

Changa ni chako nutenge mwamakani


You on my side whenever I'm down

Safunika wina ayi

Angakongole alibe wawo mwayi

Kalilole ukamuyang'ana

Othwanima kuposa mphenzi mami

Wakomedwetsa neyo khalangati


Omandikonda neyo (ndiweyo)

Wapamtima panga (ndiweyo)

Misonzi unachosa (ndiweyo, ndiweyo, ndiweyo)

Omandikonda neyo (ndiweyo)

Misonzi unachosa (ndiweyo)

Wapamtima panga (ndiweyo, ndiweyo, ndiweyo)

Iwe


Soni tabwera niku vinitse

Wadada wako tiwadziwise

Suzgo nivintchi nipuliskike

Pano pacharo nkhutemwa ndine

Oh it's a wedding day iwe ndi ine

Mu chi memory lane (mu chi memory lane)

Ma hater onse chimpeni

Oh it's a wedding day (it's a wedding day)

Iwe ndi ine (iwe ndi ine)

(Aaaah aaah aaah)

Muchi memory lane


You on my side whenever I'm down

Safunika wina ayi

Angakongole alibe wawo mwayi

Kalilole ukamuyang'ana

Othwanima kuposa mphenzi mami

Wakomedwetsa neyo khalangati


Omandikonda neyo (ndiweyo)

Wapamtima panga (ndiweyo)

Misonzi unachosa (ndiweyo, ndiweyo, ndiweyo)

Omandikonda neyo (ndiweyo)

Misonzi unachosa (ndiweyo)

Wapamtima panga (ndiweyo, ndiweyo, ndiweyo)

Iwe


You on my side whenever I'm down

Safunika wina ayi

Kalilole ukamuyang'ana mami

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status