Loading...

Download
  • Genre:Others
  • Year of Release:2024

Lyrics

Mmmmh this one's for you

And only you baby


Yemwe angathe kufotokoza

Momwe Ndimamvera


Ase Hyke


Palibe mawu amene ndingagwilitse ntchito

Pokuuza kapena pokulembela nyimbo

Omwe angathe kufotokoza momwe ndimamvera


Momwe ndimamvelela za iwe momwe ndimamvelela

Momwe Khristu anakondela tchalitchi

Momwe Yudasi anakondela ndalama

Momwe mwezi umakondela uyenda nchithuzi thuzi

Ndi momwe inenso

Nzakukondele Daling'i


Ngati uzakhetse msozi uzakhale wa chimwemwe

Suzamvaso dzina lina ndikale wa iwe wekha

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina


The way you make me nervous ndikuzandidekhesa

Let me know you're right here when I'm feeling under pressure

Zoti ndinakasamba patipo sindimatha kumvesa

Cause the chance was like one to a million baby

You're my one in a million

Yeah it's you

That's on my mind all day even when you're far away

Yeah it's you

Mtima wanga umadumpha everytime I hear your name

Yeah it's you

Nkhope yomwe ndimaona everytime I close my eyes

Yeah it's you yeah it's you girl it's you


Ngati uzakhetse msozi uzakhale wa chimwemwe

Suzamvaso dzina lina ndikale wa iwe wekha

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina


(Guitar solo)


Uzakhale wachimwemwe

Ndikhale wa iwe wekha


Ase Hyke


Dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

Suzamvaso dzina lina

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status