Loading...

Download
  • Genre:Others
  • Year of Release:2024

Lyrics

Oops on the board

Louder

Kupeza omukonda ndikhala pa low, pachuluka afiti pa mudzi pano

Kupeza ka dollar ndikhala pa low

Anthu akangoziwa ngini yanga ili bho, ati wazitenga kuti uyu

Wazitenga kuti

Wazitenga kuti uyu, wazitenga kuti

Mukauzane aah mukatutane ah

Mukauzane aah mukatutane

Osatila moyo wanga mma status, ndikuzizimusani

Akadziwa zikuyenda aku hater, ndikuzizimusani

Ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)

Ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)

Angodabwa save the date, angodabwa ndili ku states

Angodabwa save the date, angodabwa ndagula benz

Paja munandipasa malire, izi Singafikile

Paja munandipasa malire eeh, singafikile

Mukauzane aah mukatutane ah

Mukauzane aah mukatutane

Osatila moyo wanga mma status, ndikuzizimusani

Akadziwa zikuyenda aku hater, ndikuzizimusani

Ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)

Ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)

Sangaononge chinthu chomwe sachiziwa

Ndisanatchuke anthu asanandidziwe

Zanga zinkandiyendela, Mbuye ankandikondela

Olo babe yanga simmene inkandikondela

Koma dalitso wina umabwela ndi ziphinjo

Nthawi yopemphela ndikumakhala ku show

Anzanga anachuluka sindikhala pa door

Satana naye ali busy kuti andimalize

Poti za moyo wanga akuziziwa mwa easy

Ndeno ndapanga chi sankho, kuti ndizipatule

Ena aziti ndi sankho

Ndikuphusha hustle apa ndinagula Passo

Sindinena chikubwela koma anthu azizwanso

Mukauzane aah mukatutane ah

Mukauzane aah mukatutane

Osatila moyo wanga mma status, ndikuzizimusani

Akadziwa zikuyenda aku hater, ndikuzizimusani

Ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)

Ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)

Ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)

Ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status