Bello Child ft. Mellz & Thinka Spark Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
Hahaha Sizonke neh
Relo nde
BigWill did it
Anthu ambili kutukwana chani
Kuti nfana ameneyo akuzilimbisa mtima ndi chani
Timavala bello (yeah)
Olo muyankhule bwanji koma ifeyo nda bello (louder)
Singavale thonje (koma)
Staff yokuti ku scanner kumabwelesa zitenje ase
Guntolah iweyoo
Ngati wina sanamvese bweleze
Ngati alipo amandiposa ndioneseni
Ndione sneaker, ndione t-shirt, ndione chain
Yemwe wavala tunduma muwowozeni (woooh)
Bello child ase, bello shit
Ghetto child ase, ghetto shit
Pant wangayu ndi bello
Sneaker ndi bello
Shat yangayi ya bello
Tunduma ndi zero, bello shit
Ndati iwe, ndi bello shit
Eeh look
Gang yangayi ndi bello, imavala bello
Nkazi wanga so wa bello, velo tinagula bello
Ma bulangete ndi bello
Sindingafunde chipiloni
Olo ndiwoso za bello
Timachina kugula ma parts sitimayezesa ka kilo
Chilichonse ndi bello
Chingabwe kusuta chi bello
Olo kupita ku jail, tikatuluka pa bail
Condom mpaka ya bello?
Eh ma husha analowa bello plain pyuuu aviator bello eh
Anzanga ndachina Brongman
Ndine katundu wa boma
Ndina conquer (KNQR) achina Hayze, amanditcha dobadoba
Mudya koma mochedwa
Chifukwa akazanu ndiku nyoba
Look at my drip, look at my swag
Bello child mboba
Dreadlocks bello, phone yanga yi ndi bello
KNQR bello, ife tundumayo zero shit
Ngati wina sanamvese bweleze
Ngati alipo amandiposa ndioneseni
Ndione sneaker, ndione t-shirt, ndione chain
Yemwe wavala tunduma muwowozeni (woooh)
Bello child ase, bello shit
Ghetto child ase, ghetto shit
Pant wangayu ndi bello
Sneaker ndi bello
Shat yangayi ya bello
Tunduma ndi zero, bello shit
Bello, kaunjika shit
Ife timavala bello wamva et
Singasiye kuvala bello, ife ndi bello mpaka kalekale lo
Am icon dis bello
Ndinabadwila ndi kukula ndi kuvala bello
That's why am a bello child
From da ghetto to da whole world
Ndimavala bello up and down (yea yea)
Fashion over jeans wa dirty dirty (palibe kukukopela)
Caps ya Gucci, belt wa Gucci
Ndekuti shoes ndi Gucci
Bello shit OG staff, anti tunduma ase
Ma wise tizipeleka rip Martse
Ma wise tizipeleka rip Martse (too ghetto too gutter)
Bello child ase, bello shit
Ghetto child ase, ghetto shit
Pant wangayu ndi bello
Sneaker ndi bello
Shat yangayi ya bello
Tunduma ndi zero, bello shit
(Mbali yakuno mbali yaku no) bello shit
(Aone nawo aone nawo) Bello shit