Loading...

Download
  • Genre:Others
  • Year of Release:2023

Lyrics

Louder, koma Guntolah iweyoo eh

Tangokumana dzulo mu Limbe, ati wandikonda kale

Tangocheza two days ati wandikonda kale

Sakudziwa kuti ndine chitsilu ase, ukanandidziwa kaye

Sakudziwa kuti ndine chitsilu ase, ukanandidziwa kaye

Angoyesa wapeza chi deal ase, ukanandidziwa kaye

Ngati wakonda wakonda chitsilu ase, ukanandidziwa kaye

Usafele looks ah, koma ukanandidziwa kaye

Usafele swagger, ah koma ukanandidziwa kaye

Ma post apa IG IG, iwe ukanandidziwa kaye

Usafele HD HD, iwe ukanandidziwa kaye

Ma post apa TikTok aah, ma videos anga

I think anamva zama achievements anga

Sandi dziwa koma Akuti wandikonda

Tangokumana dzulo usiku, ati wandikonda kale

Tangocheza two days ati wandikonda kale

Sakudziwa kuti ndine chitsilu ase, ukanandidziwa kaye

Sakudziwa kuti ndine chitsilu ase, ukanandidziwa kaye

Angoyesa wapeza chi deal ase, ukanandidziwa kaye

Ngati wakonda wakonda chitsilu ase, ukanandidziwa kaye

Ukanandidziwa kaye, mwina ukanandituluka

Ukanandidziwa kaye apa kukakilana kuchuluka

Ukanaziwa ndimadumpha ma speaker

Za mkati undipeza ndili mtika

Ukanadziwa simchedwa kunsika

Ngati ndikufuna suchita

Ndimakonda kupanga come ndikupita

Ndiye utha kuyesa ndiku cheater

Koma ndikudziwa ndikuchita

Zopanga post ndimakana, mahope angazakwiye

Mungadye ndikuthawa kundisiya wamasiye

Ondifila kundisiya inuso mutandisiya

Koma ngati sukwanisa

Zitayeni tizi tchila

Tangokumana dzulo usiku, ati wandikonda kale

Tangocheza two days ati wandikonda kale

Sakudziwa kuti ndine chitsilu ase, ukanandidziwa kaye

Sakudziwa kuti ndine chitsilu ase, ukanandidziwa kaye

Angoyesa wapeza chi deal ase, ukanandidziwa kaye

Ngati wakonda wakonda chitsilu ase, ukanandidziwa kaye

Tangokumana dzulo usiku, ati wandikonda kale

Tangocheza two days ati wandikonda kale

Sakudziwa kuti ndine chitsilu ase, ukanandidziwa kaye

Sakudziwa kuti ndine chitsilu ase, ukanandidziwa kaye

Angoyesa wapeza chi deal ase, ukanandidziwa kaye

Ngati wakonda wakonda chitsilu ase, ukanandidziwa kaye

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status