Loading...

Download
  • Genre:World Music/Folklore
  • Year of Release:2023

Lyrics

Tsogolo - Lulu & Mathumela Band

...

Le le le le le le, la la la le

La la la le, la la la le

Le le le le le le, la la la le

La la la le

Ambiri pondiyang’ana

Ngati aona satana, ena mundiseka

Ena mundinyogodola, ena mundidelera, ena musilira.

Koma minute chikondano chanu chindilimbitse mtima kukhala padzikoli hi hi

Moyo wanga sichizolowezi koma ntchito imodzi yaikulu mmaigwira ah ah

Tsogolo ndiliona, ndilowala langa ndilotheka

Mwalikuta ndi golide

Tsogolo ndiliona ndilowala, langa ndilotheka

Mwandichotsa patali

Tsogolo ndiliona, ndilowala langa ndilotheka

Mwalikuta ndi golide

Tsogolo ndiliona, ndilowala langa ndilotheka

Mwandichotsa patali

Machimo omwe ndimapanga, mundipatsabe moyo, muli nane cholinga

Masiku onse moyo waka mbu ye musanditaye, ndili ndinu otetezedwa ah ah ah

Dalitsani anthu ochepawo, omwe amandikonda, nakonda ntchito yanga

Mdalitsenso anthu of ana nane, ofunika nzivutika apatseni zosowa kooma

Tsogolo ndiliona, ndilowala langa ndilotheka

Mwalikuta ndi golide

Tsogolo ndiliona, ndilowala langa ndilotheka

Mwandichotsa patali

Tsogolo ndiliona, ndilowala langa ndilotheka

Mwalikuta ndi golide

Tsogolo ndiliona, ndilowala langa ndilotheka

Singani moyo wanga Tate

Pulumutsani onse okhulupira inu

Ambiri anditemberera m’mayankhulidwe awo, ati ndilibe mwayi

Mwayi omwe ndimadziwa ine,

Kukudziwani Tate kupha munthu ndakana

ah ah

Siliva ndi golide, ndi zanu mbuye wanga ine ndi mwana wanu, kooma!

Tsogolo ndiliona, ndilowala langa ndilotheka

Mwalikuta ndi golide

Tsogolo ndiliona, ndilowala langa ndilotheka

Mwandichotsa patali

Tsogolo ndiliona, ndilowala langa ndilotheka

Mwalikuta ndi golide

Tsogolo ndiliona, ndilowala langa ndilotheka

Mwandichotsa patali

Tsogolo ndiliona, ndilowala langa ndilotheka

Mwalikuta ndi golide

Tsogolo ndiliona( le le le le le, la la la la le, la la la le la la la le), ndilowala langa ndilotheka

Mwandichotsa patali

Tsogolo ndiliona (oh)

Ndilowala langa ndilotheka

Mwalikuta ndi golide,

Tsogolo ndiliona, ndilowala langa ndilotheka mwandichotsa patali...(tsogolo ndiliona....)

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status