Loading...

Download
  • Genre:World Music/Folklore
  • Year of Release:2023

Lyrics

Ungondibwelenzera - Lulu & Mathumela Band

...

Nkhope Yako yasintha

siyomwe ija ndimadziwa,

siyomwe unkandiwonetsa pondifuna,

malankhulidwe asintha, wayamba kukweza mawu simomwe unkandilankhulira pondifuna, unkakamba mawu a nzeru Kumandilonjeza za zambiri munalipo ambiri koma iwe kundiwina

unkakamba za nzeru mawu Ako olimbikitsa papita nthawi ndifuna ndimveso kawiri

chorus

honey honey ooo

sinfuna chinthu china

ungondibwerezera(zimene unkandiuza ndisanakulore)

honey musachotsere mawu kapena kuonjeza

ungondibwerezera zimene unkandiuza ndisanakulore

honey honey ooo

sinfuna chinthu china

ungondibwerezera

zimene unkandiuza ndisanakulore

honey musachotsere mawu kapena kuonjeza

ungondibwerezera

Kodi mphete njotani ? yakusintha mtima honey chindivekereni sumasamala za ine yophaipha

unasiya kundipatsa nthawi

ntchito yachuruka poti takwatilana

nthawi yachibwenzi unkapezeka mkati odala ndine

uNandilonjeza zambiri honey unandilimbirsa mtima honey

koma mpaka ndimukalamba olo chimodzi sindikuona honey

unkandinong'oneza mwa Chikondi

unkandiphinyira diso limodzi papita nthawi ndifuna ndimveso kawiri

chorus

honey honey ooo

sinfuna chinthu china

ungondibwerezera

zimene unkandiuza ndisanakulore

honey msachotsere mawu kapena kuonjeza

ungondibwerezera zimene unkandiuza ndisanakulore

honey honey ooo

sinfuna chinthu china

ungondibwerezera

zimene unkandiuza ndisanakulore

honey musachotsere mawu kapena kuonjeza

ungondibwerezera

ukamandiyankhula ngati wina ukandiyang'ana ngati wina

kundisekelera komaliza mpaukwati

oweee

papita nthawi usanabwereze

chorus

honey honey ooo

sinfuna chinthu china

ungondibwerezera

zimene unkandiuza ndisanakulore

honey msachotsere mawu kapena kuonjeza

ungondibwerezera zimene unkandiuza ndisanakulore

honey honey ooo

sinfuna chinthu china

ungondibwerezera

zimene unkandiuza ndisanakulore

honey musachotsere mawu kapena kuonjeza

ungondibwerezera

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status