Loading...

Download
  • Genre:World Music/Folklore
  • Year of Release:2022

Lyrics

Nthawi - Lulu & Mathumela Band

...

Nthawi yatha tiyendereni

chikondi Chatha tithandizeni

mukatiyendera zinthu zimayenda

maumboni tili nawo angapo

ndachepa ine,inuyo mukuleeee

mwandilimbisa monga njanji

kusenza zitonzo zochuluka

pa ntchito yomwe inu mudandipasa

ndilinazo ine zitsanzo zambiri

ambiri mudawadusisa

ambiri atchukanso ndi zoipa

zoipa n'kumatandidwa nazo

tilimbiseni ife kukhala m'chiyero

poti n'chifanizo chanufe

Nthawi yatha tiyendereni

chikondi chatha tithandizeni

nkhondo zakuthupi tinayesa

Zina kuwina koma kubwera oguja mano

mbuye wathu tithandizeni

ubale wathu watha tilumikizeni mbuye

madalitso anu abwere ndi mtendere

abale asamapemphe kugwa kwanga

anzanga kumafuna nditagonja

kodi nyumba yawo ya mtundu chani

afuna atagwesa Kaye yanga

mulipo ambuye mulipo

suyu ndili moyo

komabe aphunzitseni azidikira pa inu

Nthawi yatha tiyendereni

chikondi chatha tithandizeni

(nkhondoyi ndi yanu)

nkhondo zakuthupi tinayesa

Zina kuwina koma kubwera oguja mano

mbuye wathu tithandizeni

Asiye machitidwe oti akomere inu Tate

afuna kukomesa za m'dziko owooooh

koma n'kayang'ana nthawi

n'kasanthula malemba

ndi zizindikiro za kumapeto owoowu woh

Nthawi yatha tiyendereni

chikondi chatha tithandizeni

nkhondo zakuthupi tinayesa

zina kuwina koma kubwera oguja mano

mbuye wathu tithandizeni (x3)

Easy and understandable lyric

song sing by Malawian legend(Lulu, Mathumela Band)

Lyric conceded by Chikondi R J Million (From Mj in Malawi)

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status