Ndalimba Mtima
- Genre:Afro Soul
- Year of Release:2024
Lyrics
NDALIMBA MTIMA
Oh oh oh
V1
Chinthu chimodzi ndipempha Yehova
Nkhazikike mnyumba yanuyo
Masiku onse amoyo kuti ndione kukongola kwanu
Moyo wanga ufunisitsa kutumikira dzina lanu
Kwa anthu olengedwa anu kuti adziwe za ufumu wanu
Mtima mwanga ndilakalaka kuphunzitsa za mawu anu Yehova
Kwa anthu amitundu yonse iwo adziwe za mphamvu yanu
see lyrics >>Similar Songs
More from Synord
Listen to Synord Ndalimba Mtima MP3 song. Ndalimba Mtima song from album Ndalimba Mtima is released in 2024. The duration of song is 00:03:47. The song is sung by Synord.
Related Tags: Ndalimba Mtima, Ndalimba Mtima song, Ndalimba Mtima MP3 song, Ndalimba Mtima MP3, download Ndalimba Mtima song, Ndalimba Mtima song, Ndalimba Mtima Ndalimba Mtima song, Ndalimba Mtima song by Synord, Ndalimba Mtima song download, download Ndalimba Mtima MP3 song