Loading...

Download
  • Genre:Hip Hop & Rap
  • Year of Release:2022

Lyrics

Amakukonda ft. Charisma - Gwamba

...

potilenga analenga ofanana naye

yaaah

tonse ndamodzi sifeosiyana ayi

yaaah yaaoh

konda zanko mene uzikondera iwe mwini

yaaah

chonde osamasilira chithu chamwini

ambuye amakukonda (konda)

nthawi yako ikubwera (bwera)

ambuye amakukonda (konda)

nthawi yako ikubwera (bwera)

aaaaaaah

panjira zonse ndinasakha yachidule (yeeh)

machimo achuluka wina anditure(yeah)

koma zikavuta ndamadzuka ndkugwda(iiaah)

dzina la yesu lokha ndilimene ndingatchule

kona ndamakhala pa low

ndamuuza satana no

nkhani zotsatana no

ndili ndi yesu pa door

kona ndimathoka mayooh

uyenda ndi yesu ndi bhoh

uyenda ndi yasu ndi Go!!

uyera mtima ngati snow

yeah yeah

ndeosamaluza focus

kudzuka mawa kuvaya ku church

kupasi nditaponyeza all star

nde ngati kuli chi show

dzina langa ulipeza pa poster

ndati ngati kuli show dzina langa ulipeza pa poster

ndati yiiiih

potilenga analenga ofana naye

yaaah

tonse ndamodzi sife osiyana ayi

konda zanko mene uzikondera mwini

chonde osamasilira chithu chamwini

ambuye amakukonda (konda)

nthawi yako ikubwera (bwera)

ambuye amakukonda (konda)

nthawi yako ikubwera (bwera)

osamakomedwa ndizithu za dziko

pa maso pa mulungu tonsefe ndi equal

popembedza mbuye osakhala ndi ignore

popembedza mbuye osakhala ndi ignore

osamakhala ndi tepa

chimolo kumalizemba

sikamvuta say you pray

sikamvuta say your prayer

kona ndimakhala ndi confi

dziwanda kubwera kupatsa makhofi

chifani fani ngati ndimabrosic

ndati

chifani fani ngati ndimabrosic

ndati yiiih

potilenga analenga ofanana naye

tonse ndamodzi sifeosiyana ayi

konda zanko mene uzikondera mwini

chonde osamasilira chithu chamwini

ambuye amakukonda (konda)

nthawi yako ikubwera (bwera)

ambuye amakukonda (konda)

nthawi yako ikubwera (bwera)


lyrics by @madalitso chubwe

on facebook

Similar Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status