Loading...

Download
  • Genre:Hip Hop & Rap
  • Year of Release:2022

Lyrics

My Daily Worship ft. Nimix - Gwamba

...

I have never seen no one like you

No one like you

No one like you yesu

I have never seen no one like you

No one like you

No one like you yesu

Ambuye ambuye

Ndikuthokoza ambuye

Ambuye ambuye

Ndikuthokoza ambuye


Iye ndi nyimbo ya Fuko Langa my dairy worshi

p

Ndikuvutika sumunandisiye chonchi

Kundionesa ufumu wanu kundipasa chi plot

Nde kulikonse ndikapiteko tili limodzi

Abare ndi alongo zikavutata amathawa

Mavuto pamtendere simumasintha ma color

Nde zingavute bwanji ndimayesesa ndisadande

Poti masiku sakoma onse ndi nthawi chabe

Iyi ndi dairy worship

Nyimbo yafuko langa

Winawe ukamvera uzioezamo kabata

Osamathangira kunena kuti sanayankhe

chi fukwa olo pweya tikupumuwu ndiwake

Pali chinthu chimodzi chomwe mumalakwisa braz

Mukufuna mudware kaye kuti muyanikire nthanzi

Wina amwalire kuti muyamikire moyo

AKachedwa kuyankha mumasiya kukhala royal

Ndeno tate wanga

Ndikufuna kukhala munthu wa humble

Poti ndikuziwa mumapasa munalanda

Komanso ndikufuna ndikhale chisanzo

Fana wamature poti chibwana chimalanda

Kuchepesa anger

Bible likhale nzanga

Munthu kundiyamba ine kukhulula nsanga

Kupewa ma blanda

Jah jah mumtima mwanga

Tsiku lomaliza kuchongesa zina langa


Chorus

Ambuye ambuye

Ndikuthokoza ambuye

Ambuye ambuye (zikomo)

Ndikuthokoza ambuye

Aaaah ya ya


I have never seen no one like you yesu

Chorus

Similar Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status