Loading...

Download
  • Genre:Hip Hop & Rap
  • Year of Release:2012

Lyrics

Malamulowa ndi amu ghetto, Awa ndimalamulo khumi amu ghetto(one)

Kusunga chisinsi nkofunika, khambakamba akhalila deal zikanika

Zikanika zinthu zoti zikanachitika

Osathokathoka mfana lamulo loyamba(two)


Mmdani wako amakhala nzako

Mtima wa nzako mfana ndi tsidya lina

Khomele khomele zoba amakoma mmaso

Ukatembenuka akuponyela chilaso(three)


Zomwe zili nthumba sitikamba, osa banger nazo zose zina mfana shava

Business, ndima chick aise sizimvana

Akazi ambiri achulukawa iwe ndi mbava

Umapeleka zose mmaso muli gwa(four)


Chenjela ndi mfana okupopa

Khambakamba gagadiwa zambiri angothoka

Ngati muli pa bhawa cholinga kukukawa

Zambiri angokamba Mfana yemweyo ama disser (five)


Nsanje pa Malawi ilibe nzake, ngati zikufwamba auze sizikufwamba

Nkhondo ndi anasi ndi omwewo azakufwambe

Kukufwambafwamba pamapeto mfana kape

Samala mfana, iwe dziko ndilachabe (six)


Osakongozana pa chizake

Business aise ndichinzake sizimvama

Business aise ndima frenzo sizimvama

Mapeto ndichidani, six watsatana(seven)


Deal, simangopheduka yokha

Pamakhala mfana winawake wakathoka

Mfana wake sungamganizile ndiwachikoka

Yang'ana mu crew bwinobwino muli njoka (eight)


Za mkazi wako nzakozako

Kaya mwayambana zisafike kwa anzako

Ndi mkazi wako, nkaziyo si wa anzako

Ukapusa uzadabwa akugwidwa thako(nine)


Akatchula mtengo take it easy, ndioyambila kakamila atsitsila

Ugula half price, imeneyo ndi ghetto price

Ngati ufuna kuphesa ngini usaphese ghetto

Pita kwinaku you get the double price (ten)


Lamulo lofunika kuposa ose, lamulo loyamba lotsiliza zolamula

Opa Jah Jah ika Jah patsogolo

Opanda Jah Jah iwe palibe tsogolo

Tsogoza Jah Jah, Jah Jah patsogolo


Malumulowa ndi amu ghetto

Malamulo khumi amu ghetto

Malumulowa ndi amu ghetto

Awa ndi malamulo khumi amu ghetto


Malumulowa ndi amu ghetto

Malamulo khumi amu ghetto

Malumulowa ndi amu ghetto

Awa ndi malamulo khumi amu ghetto


Uhuh! Umvese mfana

Fredokiss sakufunika kuti akhale ndi grey hair, akhale ndi imvi kuti umvesese

You know, zingini izizi ndangoziona muti zaka tochepa timene ndakhala mu ghetto

Kwambiri aise mphwanga

Uyang'anisise uyang'anisise


Ukamvesesa sunga plucke iyayi(yeah)

Maso muli nawo koma mafana simuku checker iyayi

Makutu mulinawo koma simukumvesela mwa khenge iyayi

Kiss

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status