Nzeru ft. Suffix, GD & Lilia Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
Nzeru ft. Suffix, GD & Lilia - Fredokiss
...
Anapempha nzeru,
Anapempha nzeru!!!! mfumu solomo
Let's go,
Sanapemphe mkazi ena ndasatana
pamaso ngat ngelo koma mkati muli drama maka slay queen umbanda masana
kukuswela mtima kukudyelaso ndalama
sanapemphe kutchuka zimadzetsa matama
kudziona udolo aliyense ndimwana
kunyoza fans yomwe imakuphusha padzana
waiwala zinthuzi ndizongothandizana
sanapemphe ma frenzo, ma frenzo amanama kumakusekelela ukupanga chibwana nde
chibwana chija chimadzabalaso mwana nde amadzatembunukaso nkumakuseka
sanapemphe luso, Luso limazunza
limachuluka fans yongofuna kuku user
sanapemphe chuma ukhoza kuchi luza
sanapemphe Njale, Zovala
Solomo anapempha nzeru
Sanapemphe chuma
sanapange phuma, anapempha nzeru
sanapemphe banja , sanapemphe kusanja
anapempha nzeru
sanapemphe izi, sanapemphe izo anapempha nzeru×2
Sanapemphe mphamvu
sanapemphe udindo
null