Mtima (Remix) ft. Kelvin Sings & Kell Kay Lyrics
- Genre:R&B
- Year of Release:2022
Lyrics
Inde atani kapirile
Koma osati nkanamizire
Kuti chikondi chipitilile
Wandisandusa wamasiye siye siye
She's always talking something
Even when I do nothing
Zofooka Zako sandusa lupanga Khalidwe lako nde landiopsa
Passive aggressive no more
Masiku ake si anowa chombo changa ndi Manga namondwe wamu tima ndi kamba
Mtima napereka onse
Nawerengera zala zonse
But I didn't know u will be one of us that will tear us apart there for my heart
Zamumtima mu mtima mu mtima
Mtima mwanga mwazaza revenge ndikufuna ndi takhala ndi iweyo
Koma muli mdima
Mu mtima mu mtima
Remember how we used to kiss every night and there by the beach
U were my ride ride or die
U were my ride ride or die
Ndaseguka maso ndilibe chilakolako
Ukandiseweresa unkanfipangaso chipako
Zofooka zanga pa radio ya kazako
Chonde pano panga Zako
I wish I could pretend to love you
But my heart can't recomend
Kungofuna revenge
Oh oh ziwalo Zako sizikufunaso
Mayi wanga sakufuna so
Azangaso sakukhumbaso
Maloto angawa sakulota