Loading...

Download
  • Genre:Soul
  • Year of Release:2022

Lyrics

Ooh yeah ooh yeah ooh yeah


Mphatso munandipatsayi

Ena amayesa ndi udolo wanga

Akati andipope nnati

Teddy ndi dolo palibeso mphwanga

Zonse izi amanenazi

Pena zimandisokoneza ubongo wanga

Kuyiwala izi zonse

Ndima shiner nazozi munandipatsa ndiinuyo baba

Nde ndimayamba kuzifila

Ndikamayenda anthu aziziwa

Nthawi zambiri mtima umakana

Koma matama ndi omwe anditenga ine

Ndimayamba kuzifila

Ambuye ndimayesa kuziletsa

Kuti ukulu wanu uzioneka

Koma matama ndi omwe achuluka inu


Mundichotsele zimenezi

Mundichotsele zimenezi

Anthu aziwona inuyo

Mundichotsele zimenezi

Mundichotsele zimenezi

Ndifuna anthu aziwina inuyo

Mundichotsele zimenezi


Mundichotsele zimenezi

Mundichotsele zimenezi


Mundichotsele chi khristu chapagulu

Choziwonetsera ngati ndine spiritual guru

Form of godliness but no power

Empty clouds with no showers

Chi khristu chosamanyamula mtanda

Chomamenya ma peace treaty ndi ziwanda

Chi khristu choti chilibe sacrifice

Zero obedience only full of compromise

And I wonder why they never see you

Cause I'm always at the studio I never see you

Ndizifatsa pa mapazi anu

True authority is found pa mapazinanu Lord

In fact you don't have to do anything

I need to decide to make you my everything

In fact you don't have to do anything

I need to decide to make you my everything


Mphatso munandipatsayi, ena amaona ngati udolo wanga

Samadziwa kuti zonsezi zinachokera kwa inuyo apapa palibe changa

Akamandikweza ndimaloza kwa inuyo kuzitengala utha kugwapo nsanga

Ndi chifukwa ndinasankha kumalimbikitsa anthu mu zinyimbo zomwe ndimapanga

Nde, Tate ndikupempha muzindikumbutsa

Kuti kukhala munthu woleza sikupusa

Luso lisakhale chifukwa chomazikuza

Mtima uzinditsutsa nde zizindikhuza

Ndinaphunziranso kuzichepetsa ukakomedwa umazaiwala pena

Kuti lusoli ndi mphatso nde ndimamvetsetsa akanafuna akanawapatsa ena

Mundipatse chidziwitso ndikazindikire

Uwu ndi mdalitso ndisamazifile

Kuzimva ndikophweka ndione malire

Nzeru ndi kuzichepetsa zisatalikire

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status