Loading...

Download
  • Genre:Gospel
  • Year of Release:2021

Lyrics

Nyimbo Ikatha - Kelvin Sings

...

Kunja kwacha (mavuto ndi omwewa koma tsiku langosintha)

Mdima wagwa(nyimbo ndi yomweyi koma oyimba wango sintha)

Mtima wanga umasweka kale pena ndi yesa ngati ndilibe m'bale

Kusowa oti angandithangate

Tsogolo looneka lopuwala komabe ndiimaba(mwina mavuto nkuzilala)

Misonzi I Kamanga nyumba pamasaya

Confort me zitolilo ndi gitala

Ndikakhala chete makutu mwanga mumaveka nyimbo for some time mtimawu supweteka chowawa chimagwera mkati

Mayeselo a moyo wanga (nyimbo ndi likasa)

Nkhawa ine nkhawa ine (nyimbo ikatha)

Nyimbo ikatha (ndiyimbebe)

Nyimbo ikatha (ndimbebe)

Coz as it plays I'm alright I'm alright I'm alright

Maloto anga ndimalota ndili ntchana

Anthu ambili dzina langa akuliyitana

Mayi anga kusekelela akandiyang'ana

But later on reality strike and am back with MI fellas chilling on the block and the sun rise and it set we are watching we pray fi di blessings we grind till we hafitt but

Whom jahjah blessed though no man can curse now blage yala strum ikaso drum tiyimbe nkhawa tipachike

Poti tikakhala chete makutu mwanga mumaveka nyimbo

For some time mtimawu supweteka chowawa chimagwera mkati

Mayesero a moyo wanga (nyimbo ndi likasa)

Nkhawa ine nkhawa ine (nyimbo ikatha)

Nyimbo ikatha (ndiimbebe)

Nyimbo ikatha(ndiyimbebe)

Coz as it plays am alright am alright am alright

Mayesero a moyo wanga nyimbo ndi likasa

Nkhawa ine nkhawa ine (nyimbo ikatha)

Nyimbo ikatha(ndiyimbebe)

Nyimbo ikatha(ndiyimbebe)

Cos as it plays I'm alright am alright am alright

Similar Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status