Loading...

Download
  • Genre:Soul
  • Year of Release:2020

Lyrics

Mamuna Amene Ndili - Kelvin Sings

...

unandipeza ndili lova

ndilibe kalikonse

m'matumba mwanga mobooka

nyumba yopanda khonde

ndekuti dzuwa likawomba

nkati khuma kumaonda

iweyo utandiona

simvetsa chomwe unakondaaa


utabwera unandilimbikitsa unati ndisabwerere m'mbuyo

chomwe chinali chako nanenso ndi changa kuti ndisamasowe tulo


you must be a Saint or something

how could you give it all and ask for nothing in return now yah


ndikusowa chonena ine

malangizo ako

andifikitsa pena ine

poti ndine wako


Bwera umunyadire mamuna Amene Ndili kamba ka iwe

bwera umunyadire mamuna Amene Ndili kamba ka iwe


for i was never enough

i had room for you my bae

ndidzizwa ndi chisankho chako

chokhala nane ngakhale munyumba mwanga mpando munalibe


pomwe sizinkandiyendera

unagwada ndikupemphera

pamene mwayi unasendera

unandiuza ndimukumbuke Namalenga


ndikamabwera ku ulenje

m'malo mwa nyama ndi denje

nkumandilandirabe ndi chimwemwe ine pakamwa kakasi

you know pena nkati ndidye frus

rest of my days i am under the weather

but i believe GOD gave you to me to help me keep it together


you must be a Saint or something

how could you give it all and ask for nothing in return now yah


ndikusowa chonena ine

malangizo ako

andifikitsa pena ine

poti ndine wako


bwera umunyadire mamuna Amene Ndili kamba ka iwe

bwera umunyadire mamuna Amene Ndili kamba ka iwe

bwera umunyadire mamuna Amene Ndili kamba ka iwe

bwera umunyadire mamuna Amene Ndili kamba ka iwe


ndikusowa chonena ine

malangizo ako

andifikitsa pena ine

poti ndine wako

bwera umunyadire mamuna amene ndili kamba ka iwe

bwera umunyadire mamuna amene ndili kamba ka iwe

Similar Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status