Loading...

Download
  • Genre:Afro Soul
  • Year of Release:2024

Lyrics

CHILI PA MTANDA

V1

Analosera za imfa yake Yesuyo kumuuza peturo oooh

Uzandika katatu konse iweyo tambala asanalire

Sanali opusa Yesu Khristu ayiiii pofera tchimo la ife

Anafuna tipulumuke oyeyaaaah tikaone ufumu wake eeeeeh

Anapereka chilungamo chake eeeeh mwazi nathira nsembe


Chili pa mtanda (x4)

Chadzera nkhola la ngómbe (x3)

Kufikira pa mtanda


V2

Ndiochepa amapereka mmmh nthawi yawo kwa Mulungu

Apereka nyengo yawo iwowo ku zi ntchito za thupi uuuh eeeeh

Koma mawu amanenetsa usatame mulungu wina

Ine ndine Mulungu wako namalenga wa zonse


Chili pa mtanda (x4)

Chadzera nkhola la ngómbe (x3)

Kufikira pa mtanda


V3

Anatisiira chisomo chake Yesuyo uchimo onse anachotsa

Analasidwa natunduzidwa Iyeyo mtanda wako nanyamura

Napereka nsembe yonse kudzera pa mtanda

Napereka thupi lake kupulumutsa moyo wako


Chili pa mtanda (x4)

Chadzera nkhola la ngómbe (x3)

Kufikira pa mtanda

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status