Bars Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2024
Lyrics
Bars - D-Spencer 97
...
Yeah! 9seven
D-Spencer, The D Brotherz
Nde mwati 42 bars eti?
Choyamba ma guy ndiyambe ndi kupepesa
Tisachedwe nzolemba, sindikufunanso ka paper Sir
Ndikambe za Ambuye, zinazi ndikungobebesa
Mwa Yesu mu ndi dhilu ngakhale mukuphweketsa
Ndine mwana Chiuta, amama na ankhazi
Kupanga vya kuchanya pano nkhuona vya munthazi
Despite all the fasting koma ndikukula mwa thanzi
Kuvinila Yesu ndine bro wa Makhadzi
Ndikada ndimayera ndi ake magazi
Pali za Mulungu ndimafika, iyi ndi ntchito ya mapazi
Satan akhale uko, ndamuyikila ma bars
Pano chi mfana chiwala, atumbuka ati “Mphazi”
In God you’re safe like Joseph
Trust in yourself and tonsefe
Kweza dzina lake pa tsiku la chi seven
Ulaliki okha ukangomva 9seven
Kumenya ka pemphero ingodziwa devil ndapha
Nkangonena “Amen” ingodziwa nkhondo yatha
Nkangotchula Yesu eeh devil yekha mantha
Nkangotenga bible basi ndimamupanga murder
Lemme break it down so maybe you can get it
He always open doors kaya ndi ma gate
“Mwati Mbuye akuona?”, ine eya ali maso
Ndi zomwe akupangazi ndithudi ayimanso
So i got goals too like my friend Gabadinho
Nyota ya uzimu, mazgo nkhumwa nga ni vinyo
Ndikamenya prayer dziwa chiwanda ndichiphanso
Olo kuyankhula ndi Yahweh, pemphero nde chiphaso
Ndimapanga izi kuti adani ndiwaminitse
Kumenya ka pemphero kongotenga ma minutes
You talk about the money but you don’t pray in the morning
Ain’t difficult finding but this sounds funny
If you ain’t having Christ nde m’bale ukugona
Do you have a place in heaven? Imagine if you go now
The blood of Jesus Christ like wine it’s what i’m sippin’
The game going smoothly even if i’m sleepin’
Mbuye samalola ana ake tisafale
Ndipo sangakondwe mawu ake tisafale
Gwada, prayer, m’phwanga usafooke
Zoipa ukupangazo limakwana la 40
Wa lero ndi umenewu, apa ndingothera pompa
Zambiri ndikambabe, inu mungokhala pompo