Loading...

Download
  • Genre:Gospel
  • Year of Release:2023

Lyrics

Kondela - D-Spencer 97

...

KONDELA lyrics

9seven

Yeah (aaa aah mumandikondela)

D Brotherz, D-Spencer (aaa aah mumandikondela)

Siine wochenjera kupezeka ndili moyo

Nane sindimvetsa nthawi yomwe ndilimoyo

Madalitso mbwee, kundipatsa nditangodekha

Kupempha chimodzi ndikundipatsa double decker

Munandipatsa vep, apa ndikupeza cash

Ndikudyanso bhooo, hmm hmm Squash

Nzeru zanga zikangotha inu mmayamba pompo

Pakhudza dzanja lanu moyo ukumayenda bhobho

Zomwe ine Mbuye andipangira

Akuona ngati ndikuphangira

Nkamaona zonse mwandipatsira

Inu Mbuye wanga m’makwanira

Mumandikondela

Aaa aah mumandikondela

Mumandikondela

Inu Mbuye wanga mumandikondela

Kondela, kondela

Aaa aah mumandikondela

Kondela, kondela

Aaa aah mumandikondela

Mwawala m’moyo wanga ndithu kuposa magetsi

Mpake ndikukondwa uku ndikudropa ma verse

Mmathana ndi zina zoti ineyo nsakudziwa

Kuthana ndi nkhondo zoti ineyo sindingathe

Mmakonza njira ngati pa nyanja ndi Mose

Mpake ndikuimba olo ndikuyuza mose

Chifukwa cha inu nyengo zanga zinasinthano

Ndipo ndawonadi mau anuwa si nthano

Zomwe ine Mbuye andipangira

Akuona ngati ndikuphangira

Nkamaona zonse mwandipatsira

Inu Mbuye wanga m’makwanira

Mumandikondela

Aaa aah mumandikondela

Mumandikondela

Inu Mbuye wanga mumandikondela

Kondela, kondela

Aaa aah mumandikondela

Kondela, kondela

Aaa aah mumandikondela

Ena akufunsa, “akuimba uku ndani?”

Ena akudabwa, akuimba hook ndani

Ena kundithoka Spencer Ambuye akukondani

Moti sindidanda kuti mawa ndidya chani

Ati ndikuzipopa, ine shaaa! Eya poti,

Ndathera pa inu ngati ndege pa airport

Mwandipatsa dola, ana, mphatso

Akazi onsewa munandipatsa wanga, that’s all

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status