Loading...

Download
  • Genre:Hip Hop & Rap
  • Year of Release:2023

Lyrics

Yeah

Ndikasuta chamba chamba

Nzelu zanga zimakhwima

Komaso ndikangomwa mowa

Pena ngati nzingothima

Tandiuzeni, Chabwino Nchani

Chamba or mowa

Chabwino nchani

Chamba or mowa

Ndukanika kusankha

Chamba or mowa

Chabwino nchani

Chamba or mowa

Ndukanika kusankha

Chamba or mowa


Ndikamwa mowa akazi amaphweka

Ndikasuta chamba ndimayakhula ndekha

I got a bag full of weed

I got bottle of Hennessy

Ndikasuta chamba sinsamba ayi sinsamba

Koma Ku mowa masamba eya mmasamba

Mwina chamba chindilowetsa mutchile

Ndikamwa mowa madzuka ndi mmatsile



Ndikasuta chamba chamba

Nzelu zanga zimakwima

Komaso ndikangomwa mowa

Pena ngati nzingothima

Tandiuzeni, Chabwino Nchani

Chamba or mowa

Chabwino nchani

Chamba or mowa

Ndukanika kusankha

Chamba or mowa

Chabwino nchani

Chamba or mowa

Ndukanika kusankha


Tibanditse aise!

Ndimadekha ine ndikangobanda

Nde ndikangosipa zuthela jowa mpanda

Komaso nduma saver kwa bush d

Ndalowa mu club ndi salary tuluka ndi 2 pin

Kamowa kakangogwela ku nkhwiko

Nditha kukulemba ntchito

Ndimasanduka chi drip donor

Zizungu thoka mwa simple

Ndikabanda kujowa pa stage ku show

Thamangisa file dzuwa kulowa

Ndimadzuka pota twenty past four

Kumwa shot ndikafuna kugona

Aaaah aaaaah aaaa

Ine Trap life ndimaitengela

Life ya n'dala ndinaitengela

Ndikangoyaka ndimapepeluka koma


Ndikasuta chamba chamba

Nzelu zanga zimakwima

Komaso ndikangomwa mowa

Pena ngati nzingothima

Tandiuzeni, Chabwino Nchani

Chamba or mowa

Chabwino nchani

Chamba or mowa

Ndukanika kusankha

Chamba or mowa

Chabwino nchani

Ndukanika kusankha

Chamba or mowa!!

Similar Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status