Loading...

Download
  • Genre:Hip Hop & Rap
  • Year of Release:2023

Lyrics

Ndinkakuphwekesa poti unkakhala pambali

Ndinkangokuyesa mwina sungandithawe

Ndinkakuchedwesa kumakutaisa nthawi

Ndinkangoyesa mwina sungandithawe

Koma pano ine ndakulila

Ine ndakulila

Ineyo nde ndakulila

mmmh ndakulila

Koma pano ine ndakulila

Ine ndakulila

Ubwelele ine ndakulila

Aa aaaa aa aaa aaa


Love of my life

One of the kind

Nnali Steve wonder ndinali blind

Olo ndekha simpanga understand

Nali ndi Mvuto, nali ndi carnal mind

Chibwezi chongokhalila ma fights

Zachikondi panalibepo ayi

Pano ndataya chi dynamite

I'm just tryna make things right yeah

Kodi ngakuwine bwanji

Won't play games like jumanji

Babe tandipatse mtaji

I like the way you call me daddy

Linda bwelela, tizasungane

Ndizizakuvela, kuti tisakangane


You know the road when you missing home

You know it's cold when the sun is gone cold!

You know a lover when you let her go! You know!

Oooh oooooh oh!


Ndinkakuphwekesa poti unkakhala pambali

Ndinkangokuyesa mwina sungandithawe

Ndinkakuchedwesa kumakutaisa nthawi

Ndinkangoyesa mwina sungandithawe

Koma pano ine ndakulila

Ine ndakulila

Ineyo nde ndakulila

mmmh ndakulila

Koma pano ine ndakulila

Ine ndakulila

Ubwelele ine ndakulila

Aa aaaa aa aaa aaa



Zibwana nnapanga nnapanga zosiyana

Pano kukuitana mamie mumandikana

I need you back babe

I am missing you daily

Ndasowa zathu zose tinkapanga tinangosiyana malele

I'm on my knees, I'm begging you

I'm saying please, pano ine sindingakunamize

singakuike pa easy

Ayi ayi pano babe ine ndikupatsa iwe zose

Ndikukonde ndi mtima wanga ndi thupi langa lose


You know the road when you missing home

You know it's cold when the sun is gone

You know a lover when you let her go!

Oooh oooooh oh!


Ndinkakuphwekesa poti unkakhala pambali

Ndinkangokuyesa mwina sungandithawe

Ndinkakuchedwesa kumakutaisa nthawi

Ndinkangoyesa mwina sungandithawe

Koma pano ine ndakulila

Ine ndakulila

Ineyo nde ndakulila

mmmh ndakulila

Koma pano ine ndakulila

Ine ndakulila

Ubwelele ine ndakulila

Aa aaaa aa aaa aaa

Similar Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status