Loading...

Download
  • Genre:Hip Hop & Rap
  • Year of Release:2023

Lyrics

"It looks like you lost another one"


Yea aah!!


Mwayi susochela

Madalitso angobwela

Ndimalimbikila nde ndimaikapo mtima

Ali busy kunyoza ine ndungo winner


Wekha tangoona izi

Sizinangobwela izi

Wekha tangoona izi

Sizinangobwela izi


I'm blessed that's why I don't stress

Mwina mumadabwa ndikafika mmakometsa

Uonetsetse ndimayinyetsa

Sindipanga Zinthu ngati Ineyo ndikuyesa

Mwayi susochela pano Ndine big fella

Akufilabe bwanji zija ankati zogwela

Pano akuti ndine fitititi

Chifukwa ndumenya ma hitititi

Got so much to say

Ndungokwelabe

They chanting my name like Ali bomaye

Bitch get off my way

Stay in your lane

Sine size yako level yanga ili mmalele


Mwayi susochela

Madalitso angobwela

Ndimalimbikila nde ndimaikapo mtima

Ali busy kunyoza ine ndungo winner


Wekha tangoona izi

Sizinangobwela izi

Wekha tangoona izi

Sizinangobwela izi


Ndinayamba ndikuziwa komwe ndikathele

Talk is cheap sizose zomwe ine ndingavele

Chomwe mafana amaziwa ndikubwata

Anzanu u gangster tinatenga kwa madala

You say Trappin? But you Not Trappin enough!

I remember back in 19 i been up n about

Gave you a feature/future put y'all niggas on map

You niggas got amnesia nanga bwanji mumaiwala?

Eeeh sizinangobwela izi, we used to pray for days like these

Sizinangobwela izi, you should pray for days like these


Mwayi susochela

Madalitso angobwela

Ndimalimbikila nde ndimaikapo mtima

Ali busy kunyoza ine ndungo winner


Wekha tangoona izi

Sizinangobwela izi

Wekha tangoona izi

Sizinangobwela izi

Similar Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status