Zachi-Malawi Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2023
Lyrics
Yeah
Lawi
Jmo
Nyanja yokongola yachimalawi
Mapiri okongola achimalawi
Akazi okongola achimalawi
Going high umva phain
Ife tima konda zinthu zachimalawi
Ife timakonda chinkhalidwe chachimalawi
Ndima friends ife timacheza mwachimalawi
Ona awo zomwe zawabanda nzachimalawi
Ife tima konda zinthu zachimalawi
Ife tima konda ngini yachimalawi
Ife ndamalawi zochita zathu nzachimalawi
Ife ndamalawi zochita zathu nzachimalawi
Malawi Malawi Malawi Malawi Malawi
I love malawi i love malaaawwii
Dziko lanthu lokongola anthu ake okongola
Zochepazo timagawana pamavuto sitithawana
Kugwira ntchito molimbika nsima ili pa mphika
Kukhala kwanthu kwanthendere
Tigwadepatsi tipemphere
Ngakhale pali anthu ena amafuna zadyera (kudyera osauka)
Amafuna zawo zonkha nde ziziwayendera (muzafa osauka)
Safuna kuona nzao akukodwa
Safuna kuona nzao akukwera amaiwala umalawi mwa iwo
Ife tima konda zinthu zachimalawi
Ife timakonda chinkhalidwe chachimalawi
Ndima friends ife timacheza mwachimalawi
Ona awo zomwe zawabanda nzachimalawi
Ife tima konda zinthu zachimalawi
Ife tima konda ngini yachimalawi
Ife ndamalawi zochita zathu nzachimalawi
Ife ndamalawi zochita zathu nzachimalawi
Malawi Malawi Malawi Malawi Malawi
I love malawi i love malaaawwii
Umadziwa anthu amafunitsitsa kukhala mwantendere
Kukhala opanda tsankho kukhala limodzi ngat chibale
Kugwirira ntchito limodzi osachulutsa ndale
Osanyoza azitsogoleri kut dziko likwere
Umadziwa anthu amafunitsitsa kukhala mwantendere
Kukhala opanda tsankho kukhala limodzi ngat chibale
Kudzudzula zikalakwika osalowetsa ndale
Amasilira Malawi amasilira malawi
Eh koma ife timakonda zinthu zachimalawi
Or nyimbo zomwe timakonda nzachimalawi
Or akazi ife timawakonda mwachimalawi
Kupoto kuphaka tea akumwera zachimalawi
Malawi Malawi Malawi Malawi Malawi Malawi
Ilove Malawi ilove Malawi
Mina waku malawi
Jmo waku malawi
Mina ngu umalawi
Ife ndia malawi
Ife ndi amalawi
Ife ndiamalawi
Ife ndi amalawi
Ife ndiamalawi
Ma ma ma ma
Ma ma ma ma
Ilove malawi