Bambo a Ju ft. Bebesa & Chaos Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2023
Lyrics
Inuyo
Inuyoo
Leka liti inuyo
Inuyooo
Koma adzibambo ena
Inuyo
Inuyoo
Leka liti inuyo
Inuyooo
Bambo aju bambo aju inuyoo
Bambo aju bambo aju inuyoo
Kaya nkhaza mzaleka liti inuyo
Kaya kundidzunzaku kaya inuyo
Bambo aju bambo aju inuyoo
Bambo aju bambo aju inuyoo
Kaya nkhaza mzaleka liti inuyo
Kaya kundidzunzaku kaya inuyo
Oyii yeah
Inu tsiku silidutsa osandipekera nkhani
Inu bambo a ju kodi vuto lanu chani
Ndikati ndifunse kundimenya ngat jack chan
Munthu wanji osamvera ongokhalira makani
Bambo a ju inu ndati bambo a mose
Lero sitigona tulo tithano tili tonse
Mumangochoka pono osasiya kalikonse
Mukakakhuta mowa kumafuna mudye zonse
Bambo a ju izi zafika pondikwana
Zomakapempha kwanu akungonditukwana
Inu zomwe mumapanga mumangozunzitsana ana
Munthu wamayi kudandaula musiya liti chibwana inu
Bambo aju bambo aju inuyoo
Bambo aju bambo aju inuyoo
Kaya nkhadza mzaleka liti inuyo
Kaya kundidzunzaku kaya inuyo
Bambo aju bambo aju inuyoo
Bambo aju bambo aju inuyoo
Kaya nkhadza mzaleka liti inuyo
Kaya kundidzunzaku kaya inuyo
Yeah yeah
Moti Mdzimukonda mkazi wanu mdzimunyadissa
Nzodabwitsa mmamuuser kumbali mmakadissaa
Ndeno Mkazi amangogiva akangoona pali gwero
Inu munayamba kumphleya kani mumadzimva u aguero
Muzifunse zomwe,mukupanganzo ndizabhobho
Mukachoka mumasiya chani pakhomo?
Ntchito yolera Juu ndiyanonse a bambo nda Mayi
Mukhutisidwe nnzanuzo osangochulutsa, dama
Ngat sakukwanitsa muphunzitseni momukonda
Ndikulakwa kunyoza mkazi yemwe amakukonda
Zabwino amapanga simungamupatse or zikomo
Tsiku adzagwa ndeno mudzangoona ziii komo
Chilichonse ndingapange chimakhala choipa kwa inu
Mkazi wabwino atani tsiku ndi tsiku kundipezera zifukwa
Nkhanza zanu ndalema nazo ine thupi langa langodzadza ndimabala
Kwa inuyo mwina ndine mtengo kut mwina mwake sindimva kuwawa
Bambo aju bambo aju inuyoo
Bambo aju bambo aju inuyoo
Kaya nkhadza mzaleka liti inuyo
Kaya kundidzunzaku kaya inuyo
Bambo aju bambo aju inuyoo
Bambo aju bambo aju inuyoo
Kaya nkhadza mzaleka liti inuyo
Kaya kundidzunzaku kaya inuyo
Inuyo
Inuyoo
Leka liti inuyo
Inuyooo
Inuyo
Inuyoo
Leka liti inuyo
Inuyooo