Loading...

Download
  • Genre:Others
  • Year of Release:2023

Lyrics

SKEFFA CHIMOTO CHIYAMBI - Malawi Music

...

Ukalimba mtima kuyamba

Walimba myima kupambana

Have faith over fear

Ngati ungathe thamanga

Ngati sungathamange yenda

Ngagi sungayende kwawa

Bola uzipita chitsogolo

Mmene ukulimbika za enaaa

Pang’ono pang’ono uyambeso zako

Ukafali ndi mphanvu yambaa

Poti kukula saletsanaa

Ngati pali chinthu chowawa

Ambiri samachikonda

Chimakuthawitsira abwezi

Ambiri safuna kukuthandiza

Ndiko kuyambitsa zinthu

Nthawi zambiri umakhala wekha

Koma zikati zayenda

Ambiri ofuna kudya nawe

Ena amachulutsa mantha

Eti safuna kuyambitsa zawo

Anaphuzira za agriculture

Koma olo nkhuku imodzi alibe

Komatu pakadafundaaa

Anthuni padajiwitsa galu

Funitsitsa dzizayesera kupanga zanu

Mutakula mphanvu zitatha

Za pension kuphuzirila business

Ikangodula stress mpaka mmanda

Ngati ungathe thamanga

Ngati sungathamange yenda

Ngati sungayende kwawa

Bola uzipita chitsogolo

Mmene ukulimbika za enaaa

Pang’ono pang’ono uyambeso zako

Ukafali ndi mphanvu yambaa

Poti kukula saletsanaa

Nthawi zina chiyambi chimavuta

Kamba ka omwe ukugwira nawo ntchito

Amakuyankhula zokuopseza

Ukachoka pano ndithu ukasauka

Ine ndimkati ndinu bwana wanga

Muzimdiyankhula zondilimbikitsa

Kundifunira mafuno abwino

Mwina ine mawa mkuzatola mwana wanu

Pena amakuchotsa mwachipongwe

Amakuyembekeza udzapepesa ukulira

Osadziwa munthu umatopa

Kungotopa kuti watopa nazo

Kulimba mtima osabwerela

Iwo mbuyo muno akuti ndiwe mwana wa mwano

Kumayankhula zokutemberela

Ati popanda iwo palibe chomwe ndingachite

Mulungu wanga ali kuti

Mulungu wanga ndi wa moyo

Ngati ungathe thamanga

Ngati sungathamange yenda

Ngati sungayende kwawa

Bola uzipita chitsogolo

Mmene ukulimbika za enaaa

Pang’ono pang’ono uyambeso zako

Ukafali ndi mphanvu yambaa

Poti kukula saletsanaa

Pena mulungu akaona.

Kuti uli nako kuthekera

Koma ukukakamira pa ntchito

Amabweretsa vuto pantchitopo

Cholinga choti ukavutika

Ukakamizike kuyamba zako

Ukayamba zako amadziwa

Udzalembaso ntchito anthu ena

Ndilitu ndi mbiri aise

Ndakumana ndi zambiri pofika lero

Ndayankhulidwa zambiri zonyogodola

Ukati undigwetse mphwayi ulimbe

Mavuto ena ngongoenera

Tidutsemo kuti tikule

Anatero Napoleon Dzombe

Kudziwa njinga mkugwa nayoo

Tikagwa timangodzuka

Kusasa fumbi mkumapita

Tikaduka timayambiranso

Kulimbikira mpala tiphukenso

Ngati ungathe thamanga

Ngati sungathamange yenda

Ngati sungayende kwawa

Bola uzipita chitsogolo

Mmene ukulimbika za enaaa

Pang’ono pang’ono uyambeso zako

Ukafali ndi mphanvu yambaa

Poti kukula saletsanaa

Pakavuta pamwamba uyambirenso pansi

Bola uzipita chitsogolo

Pofuna kuyamba zako lorera kuvutika

Bola uzipita chitsogolo

Uyende ndi okhawo ovesesa loto lako

Bola uzipita chitsogolo

Alipo ena angakuphere loto

Bola uzipita chitsogolo

Mvula ubwana gwira ngati watchito

Mwayi uziuonera patali ngati chiomba nkhang..osauphonya

Bola uzipita chitsogolo

Osanyoza munthu kamba kamaonekedwe

Bola uzipita chitsogolo

Mwayi suvala suit uzangoza polemeraa

Bola uzipita chitsogolo

Aaaah

More Lyrics from Malawi Music Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status