Loading...

Download
  • Genre:Afrobeats
  • Year of Release:2022

Lyrics

GiboPearson Izathela Ma Penalty PhalombeMusic - Malawi Music

...

Malawian star

iiiiiiiiiii iyiiii

gibo piyason

phalombe phalombe music

izathela ma penalty Babie

izathela ma penalty Babie


uzangoyesa kundisiya

nzakuoengesa misala

iwe kuthesa ine kukuloza zanga chetee

usayesa kundisiya ndizakupondesa kasipa

iwe kuthesa ine kukuloza zanga pheee


izathela ma penalty Babie

izathela ma penalty Babie

awiri sangayende asanapangane

kodi wavomereza uzakhala nane

ngati usandisiya undimasuletu

undiuze chikondi chisanakuletu

Nthawi ndili nayo ndikukhansuletu

zokuti ndiwe wanga ndisamatchule

Ukadikila kuti undiyuze kenako Uzandiswere mtima

Uzandimva kuning'ina

Pobwezela sinzakumenya

kapena kukutukwana ndi mawu

Ndizakusandisa mang'ina


Nkhani ya chikondi cha ine

Izathela ma penalty Babie

Nkhani ya chikondi Cha ife

Izathela ma penalty Babie


Ukazangoyesa kundisiya

Nzakuoengesa misala

iwe kuthesa ine kukuloza zanga chetee

(Ndakuchenjeza)

Usazayese kundisiya ndizakupondesa kasipa

Iwe kuthesa ine kukuloza zanga pheee


izathela ma penalty Babie

(Nkhani ya chikondi cha ine )

Izathela ma penalty Babie


Ine ndili nganga nganganga

Pambuyo pa iweyo

Chonde osachita mantha

Ine ndimasamala zaiweyo

Kuli konse ungafune nena tipite

Chili chonde ungafune nena ndichite

Chinsikukwanisa Babie ndi chinge

Uzivala ngati SJ ndi BJ


Ine ndinatopa babie ndi natopa kusweledwa mtima

Sindiine opepela

kwaine sikosewerela

Uzandisiye ine ndisanakulakwile ineee

Tizaonesana nthawi yolila ndilibe


Izathela ma penalty Babie

Izathela ma penalty Babie

Ukazangoyesa kundisiya

Nzakuoengesa misala

Iwe kuthesa ine kukuloza zanga chetee Osazayesa kundisiya

Nzakupondesa kasipa

iwe kuthesa ine kukuloza zanga pheee


Nkhani zachikondi zaife

Izathela ma penalty Babie

Nkhani ya chikondi cha ife

lzathela ma penalty Babie


instrumental .............


Izathela ma penalty Babie

Izathela ma penalty Babie

Ukazangoyesa kundisiya

Nzakupengesa

More Lyrics from Malawi Music Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status