Ndithima Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
NDITHIMA
Ndithima
Ndithima
Ndithima
Ndithima
Kwa neighbour kwa yaka!!
Ndithima
Ndithima
Magesi athima!!
Ndithima
Ndithima
Ndalama nda sanja!!
Ndithima
Ndithima
Mabvuto pa mawa!!
Ndisova
Ndisova....
ndala kulola korola
ndasamba mmanja kuwopa kolona
mowa ubwele ndithilaaa
nkhale fuewelo akwele ndithilaaa!!!
VERSE
Koma ana azibusa kuzimva
2 months nnalibusy kuzi sunga zichumazi
Zopusa kuzinda
Pano ndikuzipepesa kuzifila ngati timati
uwili ubwele
ndamva kharzibhegi wasika
ntengo wake pano ndiukwela
maso kufila ndi high silasssi
chidiso kuti pwyuuu!!! (pyuuuu!!)
tsi tsi ngati Jay z ndingo chila ndi Nas
ma fansi a Arseno nonse pansssi
Mani-U samakonda akazi koma casssh
Eh ndizisanjaaa
ndazipeza ndekha musachulukidwe nzelu kundilangiza sindimvaaa
ndikuzipepesa ndimalilaaa
Ambuye lelo lokha mutikhululuke tisakamwe ndiku mwalila
angelo amatisamalila
Eh chibukuchi ndika reader
Kwa neighbour magesi azima
ndipase ka crate ka green man
ka plate ka nyemba nkazima
ndikabwela chaku elaz mukandipezapa zanzibar
(whooooooo!!!!!)
Fanzi ya hayinikenife timakhala ndi thanzi man
chimwemwe pasaya-sitimakonda ma stressi zo kudya ma frasi ndi zanu
Pull up & whip it & do it again
magesi akathima we chill with the gang
kutoka mma 10 koka shopa ma can kukayaka kutaveni kudzablaka pa den
(ya frend!)
HOOK
Ndithima
bar man ubwele uwili
Ndithima
bar man ubwele uwili
Ndithima
kuyenda ndi nddi nddi man
Ndithima
kuyenda ndi nddi nddi man
Kwa neighbour kwa yaka
Ndithima
(wozizilaaa)
Ndithima
(wozizilaaa)
Magesi athima
Ndithima
(ndithilaaa)
Ndithima
(ndithilaaa)
Ndalama ndasanja
Ndizimwa
(wozizilaaa)
Ndizimwaza
(wozizilaaa)
Mavuto pa mawa
Ndisova yo jamey
ye jamey.... YA!
Ndithila---chosa mu fridgi man
Ndithila---chosa mu fridgi man
Ndiblowa---eskom magesi athima
Ndibolla---
VERSE
Poketsi ya jaketi muli ka 60 ba (baaa!!!)
maboys kumenya ka bageti we fina turn up & hit the bar
changa changa
tana zulu boy- chaka chaka
mahasala mulipo kuwona wangongole kumuzemba chi- chaba chaba
malehu alimo nkhatimo koma ndawathawa tikumane- panjapa
magesi kulibe zachikulilezi inezi zochimwazitu- sindipanga
changa ndichokumwachi ndichimwa
kuhasa ma dallazi nkuziwaza
barman ubwele ndizi mikundaz
ndimamwa mwa sayizi thila full tankz
ka ganja ka wize ways kusutha feeling so nice mpaka braini kusuntha
mpaka ka breadi sindikukutha
mpaka ma bebinso sindifuna
mowa umakwana bola madamu anga nyama pa denipo- ndikukuta
masufuliya
kuyelesa mipoto surf-unilever
kodi tana ku kitchiniko muutaniko
tikusuka bale za carrier
smos- smos!!!
zakaliyaaa
ntinafuna wanga wa carreer
magesi akathima ndima yasa fridgi ndikupita panja kuka-chilla
tikaya mawa timaza chila
kulapa kumvela radio maria
dexter! kuyenda ndi nddi nddi man
mumini basi kukwela mo thithikana
LAST HOOK
Ndithima
ka jelican ka bwele
Ndithima
ka jelican ka bwele
Ndithima
Ndithila
Ndithima
kwa neighbour kwa yaka
Ndithima
eskom yathima
Ndithima
eskom ya yaka
Ndithima
Ndalama ndasanja
Ndizimwa-Toona zi dollars
Mavuto pamawa
Ndisova
ndala kulola korola
ndasamba mmanja kuwopa kolona
mowa ubwele ndithilaaa
nkhale fuewelo akwele ndithilaaa!