Loading...

Download
  • Genre:Afrobeats
  • Year of Release:2022

Lyrics

Heeeh

Yeah yeah

Yeah yeah yeah Yeah yeah yeah

Ndi trap, ndi trap yeah yeah

(Ndi trap yeah yeah)

Ndi trap, kukula kukula


Kukula ndi trap

Moyo watiwonetsa zi kwapu yeah yeah

Kukula ndi trap

Aphawi ndi ophula pali gap yeah yeah

Mavuto ndi mpweche kugwila tchito mpakana ukweche eh

Kulila ndi mpweche

Kugwa mchikondi Pena mtima usweke eeh

Mavuto ndi mpweche kugwila tchito mpakana ukweche eeh

Misozi ndi mpweche mavutowa sakutileke eeeh


When I grow up I wanna be a doctor

I will be on top of the game I think ndimkalota

Ngati mwana ndimkaganiza mokhotakhota

Kuti kumaliza geli pompo pompo kuchitola

Sindimkadziwa life is nah easy

Mapepala angowola ndimavaya Tz

Thawi yopuma imasowa ndimakhala busy

Sindimkaganizilako zozapanga business

I miss those days

Deni yawulele, phwanya ya ulele, school ya ulele, phasha za ulele,

Zonse za ulele, Pano ndinakula ndikuchita kusowa ya Mchele


Kukula ndi trap

Moyo watiwonetsa zi kwapu yeah yeah

Kukula ndi trap

Aphawi ndi ophula pali gap yeah yeah

Mavuto ndi mpweche kugwila tchito mpakana ukweche eh

Kulila ndi mpweche

Kugwa mchikondi pena mtima usweke eh

Mavuto ndi mpweche kugwila tchito mpakana ukweche eh

Misozi ndi mpweche mavutowa sakutileke eeeh


M'dala imkandiwuza afana muzaziwona

Chakudya umachikana ukuchiwona

Sizophweka kuyika nsima pa tebulo

Timavutikila pena kusalila tulo

Ndimkafuna kukula kwambiri ndili nfana

Kukula ndinakula ndikusilila umwana

Ma udindo kuchuluka mavuto kudzadzana

Moyowu siwophweka kugeli timkanamizana

Eish, I miss those days

Deni yawulele, phwanya ya ulele, school ya ulele, phasha za ulele

Pano ndinakula ndikuchita kusowa ya Mchele


Kukula ndi trap

Moyo watiwonetsa zi kwapu yeah yeah

Kukula ndi trap

Aphawi ndi ophula pali gap yeah yeah

Mavuto ndi mpweche kugwila tchito mpakana ukweche eh

Kulila ndi mpweche

Kugwa mchikondi Pena mtima usweke eeh

Mavuto ndi mpweche kugwila tchito mpakana ukweche eeh

Misozi ndi mpweche mavutowa sakutileke eeeh


Moyowu ndi Nkhondo

Mu jungle kuti upeze dollar, phwanga vala jombo

Funika machawi, kuyenda ndi thawi, speed ngati volvo

Moyo kulimba daily kukhalila magobo (Oooh)

Kukhalila magobo (Ooh Ooh)

Moyo watiwonetsa zikwapu yeah (eeh)

Pali gap yeah yeah

Ooooooh

Eeeeh eeeeeh yeah

Nanana Nanana

Similar Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status