Loading...

Download
  • Genre:Afrobeats
  • Year of Release:2022

Lyrics

Ole - PiksyMw

...

chodziwika ndi bauma

mundisiye nditchole

mundileke ndipole

nde dzikoli story?

koma moto mupole

poti enawa ndima faana

size ikukana

enafe timakwana, ati tili hot ngati summer

timachita kufupika, kuvina tikufupidwa

gain moyo kugulisa?

kufaka mpweya vina player osaplayer zikutheka cheker?

ole ole

ole ole

ole ole

ole ole

undisiye ndi tole, ole

koma moto mupole, ole

and musanditole, ole

ndie zipola?, ole ole

ndikagwira nchiuno,

umadziwa kwathu ndikuno ada

sizifunika tulo ada

timautsa nyama ndi suyo ada

anzanga wa matama ngati chule

kugwedeza thupi and success ...?

zaife ndiye musati mutchule

ndikadali nfana so wait ndikule

nde ma chick, they call me dada

nde madolo akuti mmaithadi

sindichedwa kuti moto ndipole

ngati sumandifila uzitolere

ole ole

ole ole

ole ole

ole ole

mundisiye nditchole,ole

koma moto mupole, ole

and musanditole, ole

ndizipola, ole ole

am a dancer muntima, ndimu mdima

koma zitavuta bwanji,

moto sumazima

kuyesa kukhwima, mutu wayima ndiyamwano chabe koma dolo amamudziwa dzina

kuyala ma beats no nkeka?

mupanga ma hit zophweka

ngati sakudyeka ndiomweka

ngati sali full ............?

anzako amatama ngati chule

kugwedeza thupi ngati success fully?

kupeza ife ndiye musati mutchule

ndikadali nfana so wait ndikule

ole ole

ole ole

ole ole

ole ole

ole ole

mundisiye nditchole, ole

koma moto mupole, ole

ine musanditole, ole

ndizipola

ole ole

ole ole

ole ole

ole ole

ole ole

mundisiye nditchole,ole

koma moto mupole ,ole

and musanditole, ole

ndizipola

ole ole

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status