Driemo no insurance Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2022
Lyrics
Driemo no insurance - zed music
...
It′s driemo...
Ayaa aaah aah aaaaa
Sindidziwa chomwe umandikondela sindidziwa
Ndimatolingalila koma yankho lolitalikila
Despite all my flaws, sulabadila ukhala pompo umandikondelanji choncho
Kundikonda ngati ulandila mphoto
Anakutuma ndani kuti uzindikonda chonchi
Wandithesa plan, wandithela mau ineyou
I'm never gonna break yo heart, break your heart...
Kulibe insurance for that, no insurance ×4
I′m never gonna break yo