OYAMBA ft. RASHLEY Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2021
Lyrics
OYAMBA ft. RASHLEY - MBL1646
...
Verse I
Ndabwera ndi nkhani ndati ndi nene
Ndili mu chikondi ndati ndi ulele eeh
Ndatola khasu ndi mpini omwe
Poti lero ndapeza Alamu anu
Osanama anthuni sindi madziwa chikondi chikoma chotere
Zedi ine si ndimadziwa ( aah ayi ayi)
Love is so sweet ,my baby sekelela(sekelela)
Tandigwira, you are my everything
Chorus
Baby! ndi kulumbira iwe ndi oyamba
Ku kuonetsa pakhomo
ine mboni ndi makola anga
Ndalimba mtima kwanu ndi kafika
Zonse zitheka timanga oyera
Ndi kulumbira iwe ndi oyamba
Ku kuonetsa pakhomo ine
Mboni ndi makola anga
Ndalimba mtima kwanu ndi kafika
Zonse zitheka timanga oyera
Verse II
Unapanga chisankho chondi konda kusiya onsewo
Analipo ambiri ,mwayi unandipasa
Pena sindimvetsa
Ndi ka khala sindikhuza
Maka nkamakuona ulipo kamba ka ine
Awuze malume ,azibale adziwe
Sizochedwa anthu avine
Poyamikira pa zomwe unandichitira
Baby iwe ndiye ndi ku kwatira
Chorus
Ndikulumbira iwe ndi oyamba
Ku kuonetsa pakhomo ine
Mboni ndi makola anga
Ndalimba mtima kwanu ndi kafika
Ndikulumbira iwe ndi oyamba
Ku kuonetsa pakhomo ine
Mboni ndi makola anga
Ndalimba mtima kwanu ndi kafika
Zonse zitheka timanga oyera
Aaaaah timanga oyera
Timanga oyera darling
Makolo adziwe
Makolo adziwe
Oooh oooh
Ndikulumbira iwe ndi oyamba
Ku kuonetsa pakhomo
Ine mboni ndi makola anga
Ndalimba mtima kwanu ndi kafika
Zonse zitheka timanga oyera
The End