Loading...

Download
  • Genre:Afrobeats
  • Year of Release:2021

Lyrics

Pefekiti - Namadingo

...

namadingo

ndiloleni ndi nene zoona za mkaziyu

chilichonse chili mchimake pefekiti

mlingo oyezedwa bwino

thupi logwirana bwino pachingerezi

compact

ndipo sindikusamala za mkazi wina

kupatula uyu ena ndi kuwathira doom

ma insect

kandalama ndi mapeza pa kutha pa mwezi

tizakhala pansi together kumenya ma budget

tikalipira ya nyumba ya lent kwinaku tikumanga yathu

kukabwera change shopping ku supermarket

wona zako nzanga babe palibe ichi ncha ine dekha chilichonse nchako olo yanga wallet babe uli pefekiti

yemwe amati kulibe pefekiti

akadzakakuona nkhope yako babe

yemwe amati sadaone pefekiti

pansi udindo kwa a bungwe lopezerana zifukwa kuvomereza kuti kuli ma pefekiti

yemwe amati kulibe pefekiti akadzakuona nkhope yako babe

yemwe amati kulibe wa pefekiti akadzakuona thupi lako babe

adzatula pansi udindo kwa bungwe la imperfect kuli kuvomereza kuli ma pefekiti

uli pefekiti, pefekiti

kuli kuvomereza kuti kuli ma pefekiti

uli pefekiti

514898 iyi yanga password gwiragwira phone palibe zopangana cheat I love you for real now and forever more

osandikayikira sine susipekiti

ona za kale zapita zatsala zatsopano za awiri babe no ma drama no chipwilikiti

ndipo sindingalore wina aku tchayire akuseweretse my first lady

ulemu wako risipekiti mawa tipite ku mpingo kaya ku Court tika sayine marriage certificate chimodzi modzi katundu ogula my shop umboni ndi ma receit

sizongotengana pa njila opanda protocol ( protocol) ngati malonda ogula kwa mavenda my ma street

timasuke tipange mwana azindithula adad

umadziwa ka marriage product

pang'ono ndi pang'ono babe tsiku lina tizakwera range koma lero tizikwera kwa starlet babe

uli pefekiti

( back to chorus )


yemwe amati kulibeko pefekiti akadzakuona nkhope yako babe

yemwe amati sadaone wa pefekiti akadzakuona thupi lako babe adzatula pansi udindo kwa bungwe la imperfect

kuli kuvomereza kuti kuli ma pefekiti

adzatula pansi wu chairman wa bungwe lopezerana zifukwa kuvomereza kuti kuli ma pefekiti

uli pefekiti pefekiti

iwe girl wane

girl wane

ona tumaso twako

tuoneka tuoneka ngati nyenyezi girl

yamamawa girl

tumau twako mawu twako

tumaveka tumaveke ngati angeli babe

akumwamba babe

koma yemwe amati sadaone pefekiti

adzaone nkhope yako babeeee

yemwe amati kulibe pefekiti iiiiiiiiiiiiiii


+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status