Loading...

Download
  • Genre:Reggae
  • Year of Release:2021

Lyrics

Revelations - Sangie

...

Aaah

Mmmh

Oh Lord ehh

Amayankhula zonyazitsa

Amayankhula moyaluka

Amayankhula ngat anthu osalengedwa

Aah aah aah

Chipongwe nkamwa mwawomo

Kutumbwa kwa kwaoko

Awabweletsa pagulu ngat tose ndi Ana awo

Bwanji mmayiwala

Moyo ndi umodzi

Lelo ndine mawa ndiwe

Sikuzabwela chi nvula choopsa chankokolola

Sikuzabwela chi mphepo, mphepo chongosasula

Kudzabwela chi moto,moto opseleza

Kudzabwela chi moyo,moto onyeketsa

Munda olima okha

mudzi ose umadziwa akakolola

Nkhuzi zowaza okha moto wake

Amasonkhela pa phiri anthu aziona

Nkono wakumanja

Ukathandiza mmbale

Amayesetsa kuti wamanzele udziweso

Right now one might ask,chimakhala chan?

Kodi ndinu oyamba kulandila dalitso?

Oh God

Mawa silidziwika

Zomwe uli nazo uzingoyamika

Oh Lord

Sikuzabwela chi nvula choopsa chankokolola

Sikuzabwela chi mphepo, mphepo chongosasula

Kudzabwela chi moto,moto opseleza

Kudzabwela chi moyo,moto onyeketsa

Sikuzabwela chi nvula choopsa chankokolola

Sikuzabwela chi mphepo, mphepo chongosasula

Kudzabwela chi moto,moto opseleza

Kudzabwela chi moyo,moto onyeketsa

.........

Similar Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status