Mwana Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2018
Lyrics
Mwana - Lily T
...
sembe umoyo ogula
sembe kuliye kuti tinali nayo
etisiya mwana wanga ziko lavuta
antu nayo alimba mutima matenda nayo siyosila mwana wangu ziko lavuta
antu nayo alimba mutima matenda nayo siyosila nizaku uza bwanji kuti umvele
kuti umvele
mwana
nizaku uza bwanji kuti umvele kuti umvele mwana
ohhhh
chorus
mvela mvela mvela mwana mawe mwana x2
ozisungile weka umoyo wako
uyu moyo sugula ukataika sunga utole x2
mvela mvela mvela mwana mawe mwana x2
ozisungile weka umoyo wako uyu moyo sugula ukataika sunga utole x2
uyu umoyo sugula ukautaya kuli kuti ni utole soti mwana wanga uzini mvelela
nichifukwa ni kukonda kulibe wena Sono azaku uza mwana wanga uzini mvelela x2
Sono nizachita bwanji kuti mwana ni zachita bwanji kuti umvele
back to chorus