Msemere Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Umadzazindikira
Madzi Ali mkhosi
Madzi Ali mkhosi
Umadzazindikira
Madzi Ali mkhosi
Madzi Ali mkhosi
Mwana akalilira nyanga
Ya msatsi
Msemere msemere
Msemere msemere
Imfotera
Mwana akalilira nyanga
Ya msatsi
Msemere msemere
Msemere msemere
Imfotera
Mavuto
Osamawayamba dala
Moyo ndiwophweka
Ukangovomereza
Dzana
Munapita kuuhule
Kukasaka ndalama
Mwaiwala malangizo awamama
Mwana akalilira nyanga
Ya msatsi
Msemere msemere
Msemere msemere
Imfotera
Mwana akalilira nyanga
Ya msatsi
Msemere msemere
Msemere msemere
Imfotera
Madotolo pano akuti
Mwatenga edzi
Mmh zosayenda
Ukavomereza Kuti
Chako sichanga
Ndipo changa sichako
Zizayenda.
Koma
Mwana akalilira nyanga
Ya msatsi
Msemere msemere
Msemere msemere
Imfotere
Koma Mwana akalilira nyanga
Ya msatsi
Msemere msemere
Msemere msemere
Imfotere
Umadzazindikira
Madzi Ali mkhosi
Madzi Ali mkhosi
(Eleli eleli eleli)
Umadzazindikira
Madzi Ali mkhosi
Madzi Ali mkhosi