Loading...

Download
  • Genre:Hip Hop & Rap
  • Year of Release:2023

Lyrics

Iweee, iweee


Wina afapo

Apapa tikanganapo

Wina afapo

Tipezeka tagwiranapo


Aliyense azipanga zake

Siife munthu ndi m'phwake

Aliyense azipanga zake

Siife munthu ndi m'phwake

Aliyense azipanga zake


Mukundilowatu mchala

Kundikandatu pa bala

Kuputa moto munthu ndangoKhala

Kenaka uzitititi tikukunyala


Ukumachezatu mopusa aise

Ukumayankhula mokhuta aise

Malingana ndi zomwe tikudutsa ife

Anthu tikumayenda olusa aise


Nde osamandijayila, osamandijayila

Madhala ali ndi maizemill mabwande ndikugayila

Uzindikira ukudzuka uli ku Bwaila

Mfanayu si lamya koma mmene amutchayila


You know how I be (Bee), kundiputa ndi mbola

Different kind of animal, osamandicaller (khola)

Unless ndiwe photographer,osamanditola

Unless ndiwe photographer, osamandi...


Wina afapo

Apapa tikanganapo

Wina afapo

Tipezeka tagwiranapo


Aliyense azipanga zake

Siife munthu ndi m'phwake

Aliyense azipanga zake

Siife munthu ndi m'phwake

Aliyense azipanga zake

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status