Mudyera Pansi ft. Dirty Flo Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2023
Lyrics
Mudyera pansi ft. Dirty Flo - Achina Gattah Ase
...
Ase thin achina GA yeah yeah mafa opusa kwambiri
Yo yo kubwela kwa ine mu game ndi Phatso pano rapper wako anayamba hustle ndimakhola ku show nkupatsa platform nkupatsa 50pin yakachaso (facts)
Enanu show yongokhala disco ikamatha show mwafila diso itiso yoma floper yi koma iwenso vuto Gatta akapanga show km inenso ife city iliyonse ingozaza mafanaa suwabanda ndiwe zaza ndiwe nkhwanga komabe sutiwaza uzisiyanisa creativity ndiku ngaza dissa Gatta mugetto uone mbwaza manana mwachepa ine ndinadzatu ndikudya akaz okongola kunyasatu ndipase space ndine mfana wa nasa