ZA DZULO Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2023
Lyrics
Man muli bho?
Muli nyatwa?
Koma dzulo kunayaka
Mwati muli bho?
Muli nyatwa?
Koma dzulo munayaka
Koma Muna
Eh eh eh
Koma inu Muna
Ah ah ah
Koma inu Muna
Eh eh eh
Mwati caller kutiuza matikonda inu
Mmmmmm munakondwa inu
Masten mwauza munakula inu
Mmmmmm munakondwa inu
Kumwaza dollar ngati kwanu kuli bank
2000 mwati Hank
1.5 mwati sakny
Ana a ndalama ku spread cash
Muku spend rands
Man muli bho?
Muli nyatwa?
Koma dzulo kunayaka
Mwati muli bho?
Muli nyatwa?
Koma dzulo munayaka
Koma Muna
Eh eh eh
Koma inu Muna
Ah ah ah
Koma inu Muna
Eh eh eh
Mmmmmm
Koma mayho matama
Mesa mwati kwanu kuli tractor inu
Zanyalala matayila hummer inu
Nkazi wanu mwati ndi Humber inu
Macheza ndi gunna inu
Thugathuga mwati mphwanu inu
Mwati sitigakuuuze chochita inu
Mmmmmm koma inu
Man muli bho?
Muli nyatwa?
Koma dzulo kunayaka
Mwati muli bho?
Muli nyatwa?
Koma dzulo munayaka
Koma Muna
Eh eh eh
Koma inu Muna
Ah ah ah
Koma inu Muna
Eh eh eh