Yo Maps Tizikondana Chabe Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2022
Lyrics
Yo Maps Tizikondana Chabe - Zambian Music
...
Aaha
I ya ya ya
Nana na na naaa na na
Yeee
Tulululu
Muniteme myala ngati mukalibe kuchimwapo
Munisonte vikumo ngati mukalibe kulakwapo
Iyi niziko chabe naiwe unga chimwe mailo oh
Iyi niziko tala boonse tima chimwa
Koma tizikondana chabe
Ah aaah aah ah
Koma tizinvelana chabe
Ah aaah aah ah
Koma tizikondana chabe
Chinto yako ni kunsota banzako
Ati mwaiona ija motoka bagula lelo ati uja mwaana anamwalila niwao
Bana mu faka ku business I ya ya bana mu faka ku business mmmm koma naiwe uma cimwa lyoonse pano petikamba wacosa kudala mimba nibangati bana bamene wa paya naiwe
Tikazinvelana chabe
Muniteme myala ngati mukalibe ku cimwa po
Muni nsonte vikumo ngati mukalibe ku lakwapo iyi niziko chabe naiwe unga cimwe mailo oh iyi niziko tala boonse tima cimwa coma tizikondana chabe
Ah aaah aah ah coma tizinvelana chabe
Ah aaah aah ah coma tizikonda chabe
Tima ibala cintu cimozi citi uliyense muno zico ali na ka musango anga cite bwanji cu cita teti Ali chabe naka musango ooooh oooh oh ninga ncale wo yoonda ati moonga siba madya
Ninga nkale wo ina ati onani cidumbo
Ninga nkale wo sweta ati ndiye pe baziba carolite ninga nkale wa black ati monga kulibe mafuta muuntu alibe chamushe aaaaah muniteme myala ngati mukalibe ku cimwapo
Muninsonte vikomo ngati mukalibe ku lakwapo
Iyi niziko cabe naiwe unga cimwe mailo o iyi niziko tala boonse tima cimwa
Koma tizikondana chabe ah aaah aah koma tizinvelana chabe ah aah ahh koma tizikondana chabe muniteme myala ngati mukalibe kuchimwapo muninsonte vikumo ngati mukalibe ku lakwapo iyi niziko chabe naiwe unga chimwe mailo o iyi niziko tala boonse tima cimwa koma tizikonda chabe ah aaah aah koma tinvelana chabe ah aah aah koma tizikonda chabe