Loading...

Download
  • Genre:Hip Hop & Rap
  • Year of Release:2022

Lyrics

Rebel lions warfare

It's on here

Stand under the music to understand the music


Si ine kazimvelele ongokamba za m`maluwa

Anamva anthuwa

Pa chiyambi panali mawu

Anamveka pa chimkweza mawu

Mwayi wakusintha zinthu nawu

Mphuno salota anawombela mfiti m`manja

Nde ndi ndani andigwile dzanja

Poti zatsimikizika

Zochita za anthu sizisiyanisika

Atupa mimba bwa? atadya zositika

Inu mboba

Boys out here vala zigoba

Anthu oyipa amauvala unjonda

Akaona tsogolo lako lozola komba

Pa maso akonda mu mtima azonda


Amangonama

Tigwetsa mana

Koma zochitika zimasemphana

Kwela pa nsanja zikundu nkumasekana

Dzulo kulonjeza lero kukana

Amangonama

Tigwetsa mana

Koma zochitika zimasemphana

Kwela pa nsanja zikundu nkumasekana

Dzulo kulonjeza lero kukana


Mayi koto m`baleyu si njokaluzi

Pali moto nkulinga utawona utsi

Ali pompo until atapeza nsuzi

Kunyika nsima itamangidwa mu luzi

Nde ndikufunsa

Ena akunena ndikutsutsa

Odya ndiwo ndi ena ife kwathu nkususa

Pali kwina kufasa pali kwina kupusa

Munamupha Mufasa nkani Simba kulusa

Timangomva zama audit zama report

Milandu ingofumbwa kuma court

Ndinamukhulupilira Majoti

Kutaya nkhwali kamba ka manga aka nsoti


Amangonama

Tigwetsa mana

Koma zochitika zimasemphana

Kwela pa nsanja zikundu nkumasekana

Dzulo kulonjeza lero kukana

Amangonama

Tigwetsa mana

Koma zochitika zimasemphana

Kwela pa nsanja zikundu nkumasekana

Dzulo kulonjeza lero kukana


Kutipaka nsuzi nkutijambula odya ena

Ndithudi muzakumana nayo gahena

Ankabwela pano tikawaona mpakanema

Mbiri ndiya khoswe kadya nkena

Tinamva manifesto

Kalata ya Paulo yolembela Aefeso

Tonse kukhala mtundu koma munthu ndi chileso

M`mutu modzadza mfundu ati vuto ndi chipeso

Yesa ulonjezenso

Ndi mabodza omveka bwino tatengeka

Chilungamo chenicheni tanyengeka

Ochepa za wayendela ambiri tapweteka

Amphawi taoneleledwa tapezeka


Amangonama

Tigwetsa mana

Koma zochitika zimasemphana

Kwela pa nsanja zikundu nkumasekana

Dzulo kulonjeza lero kukana

Amangonama

Tigwetsa mana

Koma zochitika zimasemphana

Kwela pa nsanja zikundu nkumasekana

Dzulo kulonjeza lero kukana

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status