Plan ft. Gwamba Lyrics
- Genre:R&B
- Year of Release:2022
Lyrics
Plan ft. Gwamba - Praise Umali
...
PRAISE
I worried all the time
and am running out of time and take air at a time
ana ndizambiri umafuna mtima
pena mantha nkudzandigwira
what if we don't make it ×2
GWAMBA
Hey yoo praise
yoo venue yomweyo ena ama floopa
samatrenda nyimbo zawo akadroopa
nde pena pride imafuna izindikopa
koma mbuye wanga sangakonde kuti ndizizikopa the rule #1 kumakhala humble piti ukazikweza amasiya kupanga zako
rule#2 osakhala ndi sankho
poti lero ndi kape mawa Ali pa mwamba
kayang'ana kumbuyo ngati ndingokuwa mbuye
ndinakhonza chan kuti inu mundimasule mwandichosa kutali kwinakuso mulambule ulendowu ndiwautali koma