Ndiululileni Grace Chinga
- Genre:Gospel
- Year of Release:2022
Lyrics
Ndiululileni Grace Chinga - Malawi Music
...
Mbuye chidalitso chi chandilemela mwachita kundikhutulila ngati mvula zomwe mwachita chakachi zachilendo umboni wanga walero upotsa wa dzulo, mbuye zomwe mwandi patsa sizanga zokha komanso ena adalitsika nazo mwandi fikitsa kutali kwachilendo komwe masomphenya anga sanafikeko. inu yehova ndiulileni zomwe munaika pamoyo wanga, Pali anthu ena akamandiona achisilira ndi ndikundinda nacho, yehova wanga ndiulileni zomwe munaika pamoyo wanga Pali anthu ena akamaniona achisilira ndikundinda nacho, (chorus) mwachizaza chikho changa chikho changa chisefuka mwachizaza chikho changa chikho changa chisefuka Mwachizaza chikho changa chikho changa chisefuka mwachizaza chikho changa chikho changa chisefuka mwala umene misili omanga nyumba anaukana nasanduka wapangodya abale ansi onse anditaya nandikumba nati ndine mwana wahule koma mbuye mwanditola mwana wanu lero zavuta andisaka andipepesa mpaka kundipempha kuti ndathandize nandinyengerera n'khale mfumu yawo. inu yehova ndiulileni zomwe pamoyo wanga Pali anthu ena akamandiona achisilira ndikundinda nacho. yehova wanga ndiulileni zomwe pamoyo wanga Pali anthu ena akamandiona achisilira ndikundinda nacho . mbuye mwandizaza mwandiza chikho changa mbuye chikho changa chisefuka mwachizaza mbuye chikho changa mwachizaza mbuye chikho mwachizaza chikho changa mbuye*4
Similar Songs
More from Malawi Music
Listen to Malawi Music Ndiululileni Grace Chinga MP3 song. Ndiululileni Grace Chinga song from album Malawi Gospel Music Best of Grace Chinga is released in 2022. The duration of song is 00:06:17. The song is sung by Malawi Music.
Related Tags: Ndiululileni Grace Chinga, Ndiululileni Grace Chinga song, Ndiululileni Grace Chinga MP3 song, Ndiululileni Grace Chinga MP3, download Ndiululileni Grace Chinga song, Ndiululileni Grace Chinga song, Malawi Gospel Music Best of Grace Chinga Ndiululileni Grace Chinga song, Ndiululileni Grace Chinga song by Malawi Music, Ndiululileni Grace Chinga song download, download Ndiululileni Grace Chinga MP3 song
Comments (9)
New Comments(9)
Dean Mkombe
Mary mulelewd5vm
This song is just a wow
Julietyasnq
it's on of my favorite song
Mildred Musondaimk5c
i love this song
official.kapebeauty
since childhood i love her songs full of wisdom
Hannah chauluka
nic
Idah mosesg9za6
i love this song
Dream Venlax
This songs always touch my soul
... One of the best song...