Nyimbo Za Mtima
- Genre:Afrobeat
- Year of Release:2022
Lyrics
Nyimbo Za Mtima - Lawi
...
Pamene ndasauka ndalemedwa mtima Bwenzi langa, limba langa limbitse mtima Pamene ndasauka ndalemedwa mtima Limba langa bwenzi langa limodzi mtima Yimba nyimbo, nyimbo ndi mtima wa chiyembekezo Timayimba nyimbo, nyimbo mpaka mtima utapepuka Timayimba nyimbo, nyimbo ndi mtima wa chiyembekezo Timayimba nyimbo, nyimbo mpaka mtima utapepukanso
Similar Songs
More from Lawi
Listen to Lawi Nyimbo Za Mtima MP3 song. Nyimbo Za Mtima song from album 30'S is released in 2022. The duration of song is 00:01:14. The song is sung by Lawi.
Related Tags: Nyimbo Za Mtima, Nyimbo Za Mtima song, Nyimbo Za Mtima MP3 song, Nyimbo Za Mtima MP3, download Nyimbo Za Mtima song, Nyimbo Za Mtima song, 30'S Nyimbo Za Mtima song, Nyimbo Za Mtima song by Lawi, Nyimbo Za Mtima song download, download Nyimbo Za Mtima MP3 song